Mabilinganya Empire - Panado ft Nepman
Name of album : Mabilinganya Singles Genre :Dancehall
Thumbnail

Click here to download this song >> Desktop | Mobile


Intro
Gafar on d board(yah)
one 2 wanthu
mabilinganya (mabili x5)
mabilinganya (mabili)
Empire laaaarge!!
Nepia dema feel defia!
Bridge (Nepman)
Aka ndika mfuti
Mpaka nakatengera tchuti(mm hu)
Ndi love ya muti
Ena kudabwa kuti ndi naka tenga kuti(ee he)

Hook (Nepman)
(Ulingati panado x2
Umandi mvetsa bwino lomwe ndika dwala.
Ulingati ndege x2
umandi tengera kutali)x 2.

Verse 1 (Jay Jay Cee)
baby ulingati jet,kapena helicopter/
Ine patient, ndiwe wanga doctor/
ine passenger ndiwe yanga motorcar/
ine chidakwa ndiwe wanga vodka/
uli fly umanditengera ku jupiter/
pankhondoyi baby ukhala victor/
ngati chinangwa si nsiya kukuta/
nane nalero mpaka thukuta/

Chorus
Verse 2 (Tamunyata)

ndakondako akazi enawa/ 
komano ndinawa siya anali ndi chikondi cho burna awa/
ndinapeza iweyo wondi chilitsa/
ndikafoka ndiweyo wondilimbitsa/
umanditengera kutali kuli nyenyezi/
umandi twanima mmaso ndiwe nyenyezi/
ndikakhala ndiwe ndimaona heaven/
Uzandi pangitsa ndikupatse ana eleven/
Bridge (Scola Fella)
(eeeh)Ulingat nyimbo za ma Rasi/
ndimafuna ndizingo mvera basi/
iwe ndi waine mpweya/
i can not live with no air/

Chorus
Verse 3 (Dotolo)

(yoh)tima sarge wez ndikabwera ndita topa/
umandifilitsa nde ndimafila proper/
chikondi sumayeza nd litmus paper/
sulakwisila dala kumandiuza dotolo pepa/
ndili ndi iwe as you wish no compulsory/
umazipereka umayenera uzilandila salary/
yes! I will commit no adultery/
akut ndina gwera makape akut nza lottery/