Bon Kavala Banda - M'dyelekezi Ngotuzuka
Name of album : Singles Genre :Gospel
Thumbnail

Click here to download this song >> Desktop | Mobile


Mdyelekezi M ngotuzuka M ngotuzuka mngotutuzuka, mdyelekezi M ngotuzuka atuzuzuka kwambiri akawona ine!!!! mdyelekezi atuzuka kaona Ine ,alekelenji utuzuka kaona Ine?akamagenda mumtengo muli kanthu.chifukwa chake atuzuka akawona ine*2 Koma mbuye walonjeza kumenyera nkhondo Ine ngati mordecai pamaso pa Harman yo!mlungu wanga walonjeza kumenyera nkhondo Ine ngati David pamaso pa goliaght yeah.

chorus

mdyelekezi M ngotuzuka M ngotuzuka M ngotuzuka. mdyelekezi M ngotuzuka atuzuka kwambiri akawona ine!! amandiona ndili ndi yes ineyo,amanditutumuka mchifukwa chake atuzuzuka akawona ine.


verse 2

adani anga atuzuka akawona ine, alekelenji utuzuka akawona ine?akamaloza mumtengo muli kanthu mchifukwa chake andiloza akawona ine*2 Koma mbuye walonjeza kumenyera nkhondo ine ngati yehosofati pamaso pa a amon wool! mbuye wanga walonjeza kumenyera nkhondo ine ngati ayisilayeli pamaso pa iguputo M mmm back to chorus.

verse 3

adani Ako atuzuka akawona,alekelenji utuzuka akawona iwe?akamagenda mumtengo muli kanthu mchifukwa chake atuzuzuka akawona iwe*2 Koma mbuye akulonjeza adzakumenyera nkhondo ngati Daniel mumdzenje lamikango.mbuye wako akulonjeza adzakumenyera nkhondo ngati achina misheck mung'anjo yamotoyo!! chorus fading