34537Downloads
Phyzix - Phee Ft Macelba (Prod. Dare Devils & Stitch Fray)
Click here to download this song >> Desktop | Mobile
Artists: Phyzix ft. Macelba
Album: ...Of the Highest Order EP.
Producers: Dare Devilz & Stich Fray
Label: It’s Only Entertainment (IOE)
(Intro: Phyzix & Macelba)
Phee!!
Phe!!/ Very Good Very Good/ We Here!
(Prelude: Phyzix)
La/ La La La La La La
La La La La La La/ ndife afana otentha
La La La La La La
(Verse 1: Phyzix)
Naturally ndine starbwoy/ am a smoking hot king sikuti m’masuta gway/ haters wonder why am still a top guy/ amandinyoza kumbali pa maso akuti hie/ ndimadana m’macheza opusa bye bye/ musamapange zanu za tulo ndi ineyo ayi/ Ndimachita manyazi kuluza am shyi/ am a born winner pita ukafuse amayi/ ine sindIzaLALA sindili ngati boat/ Flow yanga bima ma rappers ndi ma note/ Ineyo kuzatha ndi mulandu wa ku khothi/ wondiputa sangandimalize Nsanje Port
(Hook: Phyzix)
Olo mukhomelere/ Phee!!
Olo ndizidya thelere/ Phee!!
Ndife mafana o’riser basi/ timasongola mu minibus/ Phee!!
Olo mukhomelere/ Phee!!
Olo ndizidya thelere/ Phee!!
Ndife mafana otentha basi/ Kuphaka life ndi pin basi/ Phee!!
(Verse 2: Macelba)
Mfana otentha mboni yanga ndima hit
Ndanyowetsa machesi mulimbilana chilibiliti
Kundizizilitsa sizitheka
Ndine virigo pa beat funsafunsa sindidyeka
Ndizizila bwanji anzanga ndi ma hitmaker
Fanz inkakukwera kale pano unatha double decker
Anzanga ine ndi 5 okha
Enanu ndiongonamizana nkhani ngati 5 moba
Ndimakolera nanji mkandithira fire
American height koma m’chimfana chaku kaya
Mukutolera nkhuni nthawi yoipatsa moto
Iyiyi ndi real sound ya achina skeffa chimoto
(Hook: Phyzix)
Olo mukhomelere/ Phee!!
Olo ndizidya thelere/ Phee!!
Ndife mafana o’riser basi/ timasongola mu minibus/ Phee!!
Olo mukhomelere/ Phee!!
Olo ndizidya thelere/ Phee!!
Ndife mafana otentha basi/ Kuphaka life ndi pin basi/ Phee!!
(Bridge: Phyzix)
La/ La La La La La La
La La La La La La/ ndife afana otentha
La La La La La La
(Verse 3: Phyzix)
Am about to ruin your day/ ndikafika pamalo fanzi imafila tonde/ oh yeah/ u dolo wanu uli panja simungalowe munomo mumathela khonde/ all day/ I smell something fishy ngati bombe/ mafanawa ngoipa akufuna andinyonge/ Munditenge bwinotu ineyo Mundihonge/ muzindipatsa ma very good mundichonge
I work hard on MINE/ ndi kayelekela/ mafana ondigwetsa si m’mene amalephelera/ amafuna kundisala ngati wakudela/ simungandigonjetse ndinabwera
(Hook: Phyzix)
Olo mukhomelere/ Phee!!
Olo ndizidya thelere/ Phee!!
Ndife mafana o’riser basi/ timasongola mu minibus/ Phee!!
Olo mukhomelere/ Phee!!
Olo ndizidya thelere/ Phee!!
Ndife mafana otentha basi/ Kuphaka life ndi pin basi/ Phee!!