Bucci - Malungo
Name of album : Malungo Genre :Afro-Pop
Thumbnail

Click here to download this song >> Desktop | Mobile


VERSE1


Kungodzuka mamawa ongodwalika,
Ma fever ma headache Zingondiphika,
Mimba kuwila mawondowa kufoOka,
Apandingomwa Bufen ka pain killer,
Kuwona kuti sizikuthekabe,
Ma results kubwela ati matenda nje,
Ine kuzangoziwilatu,
Wakuchipatala ndauyamba akandiyeze,

(HOOK)


Si malungo,
Si zofunika panado, sikusowa kwa magazi,
Kapena ma Asazi,
Si malungo,
Si zofunika panado, sikusowa kwa magazi,
Kapena ma Asazi
Koma kusowa kwa iwe, kusowa kwa iwe, thupi langa lonseli, kusowa ntendele,
Koma kusowa kwa iwe, kusowa kwa iwe, thupi langa lonseli, kusowa ntendele,

VERSE2


Nde darling, muzipezeka pezeka,
Mukamasowatu ndimangodwalika,
Mwina sumadziwa chomwe ulitu
Mu moyo wanga kweni kweni nde fasa ndilongosola kah
Ndine nyimbo, iweyo ndi Tune oh!
Ndiwe chigoli tinakakhala football,
Ndine opelewedwa opanda iwe ndichomwe ndikunena baby, heey

(HOOK)


Mm, maso anga angofuna kukuwonaa
Hey,
Manja anga angofuna kuku ho-daaa,
Thupi langa lonseli, likufuna iwe baby,
Baby, baabyyy

(HOOK)