Andy Musiq - Wadya Mfulumira ft Blaze and Saint
Name of album : Singles Genre :Afro-Pop
Thumbnail

Click here to download this song >> Desktop | Mobile


(Verse 1) Andy Musiq


Oh oh oooh nah nah nah ye ye yeah

Kachuma kanga konse ndimafuna ndikaononge..(Paiwe)....

Chaka chino chokha ndimati ndikukwatile..

Ana awiri,atatu, odalitsa ukwati pope...

Kaukwati ka international, osati za lokolo ( lokolo eeeeh)

Koma chosadziwa ndaimbila mfiti m'manja

Kumafetsa pa tanthwe nkumayesa ndipa nthaka

Mano nditanola eeeh,

nyamandikundibisira eeh

Koma sunaziwe kutChorus(Andy Musiq)

Nali ndima plan inee (pa iweeh)

Nali ndima plan inee (pa iwe eeeh)

Koma vuto iwe wadya mfulumira, wadya mfulumira, wadya mfulumira kuchokaweh ×2 Verse 2(Saint)

Ndinkafasa ine

kuona tsogolo la mawa ndinkadekha ine

Kufuna kuona maso ankhono

Chikondi chinali cha nkhongono

Ndinkati iwe uzandigwira nkono

I had all my eyes on you

I had vision for you

Tsiku ndi tsiku kukulingalira dem real dreams for you

Sindinkafuna kukuona ukulira

I was damn serious, damn serious but u messed up see u messed babyChorus (Saint)

Ndinali ndi plan baby(pa iwe)

Ndinali ndi plan inee (pa iwe)

Koma vuto wadya mfulumira

Wadya mfulumira wadya mfulumira

Ndi plan ine, ndi plan ineeh

Wadya mfulumira wadya mfulumira

Wadya mfulumira iwe, iweVerse 3 (BLAZE)

Napepe mam mudachita phuma yeah (phuma yeaah)

Mukadasankha Chikondi osakhala chuma yeah (chuma yeaah)

Mudathamangira bwibwi kamba kazilako lako (lako)

Pomwe chakumwa chanu mudali nacho m'manja mwanu (mamie yeah)

Palibe chomwe nkanangopenya ndimaso anuwo (anuo)

Chilichonse dafunitsitsa chikhale chanunso

Mtima wazi lako lako (lako)

Mtima osilira mamie aaah yeeeh

Mwazionongera nazo banja

Akome chotani mamuna amene mu laka laka eh yeah

Chikhale chotani chikondi mufuna maka maka ayeeh

Mbali yanga ndayesesa nkhale ndimayesesabe

Koma nkutheka mamuna mufuna inuo sineyoChorus (Blaze)

Nali ndi plan ineee eh (pa iwe)

Ndi plan ine eeh eeh (pa iwe)

Mai-mai mai-mai ma yoh

Ndi plan ine eeh eh

Ndi plan aaah ah ayeah yeah

Ndi plan, ndi plan, ndi plan ine eh eh