
Click here to download this song >> Desktop | Mobile
INtro:
Blakjak,, Inde! V2... Haha,, Iwe!
Tsegula Khomo Amjiba alowe ey
Amjiba Afika,, Iwe
Tsegula Khomo amjiba aloweeh
Amjiba afika..
CHORUS
Indetu Indetu Ndinena Ndi Iwe
Tambala wachitatu asanalire
Lero Lomwe, Ndikadya kunyumba Kwako
Lero Lomwe, Ndikamwa madzi ako *2
VERSE ONE
Iwe! Usandisiye ndili Chiimire
Tabwera Uzandichi-chi-chi-chi-chi-chi Chingamire
Poti ndato-to-to-to-to-to toperatu
Komanso zonse zofunika ndaguliratu
Bwanji ukakhala ngati sukukondwa?
Kapena ukukayika zoti ndimakukonda?
Iwe ndi ine mpakana kumanda
ndipo ngati Piksy Mtima wanga Wamata..
CHORUS
VERSE TWO
Takawoneni Ka Mkazi Akoo
Kowoneka bhoo, Kopanda tsankho
Kakuti, Blakjak bwera tipange Chipako?
Ndakawuza zimenezo upanga ndi Ambuyako
Ati Blantyre Umakhala patipati??
Ndakauza Nkolokosa cha Mkatikati
Akuti, How come you FAT but you Still SMART?
Uzaziwona, ukazakhala Merchant.
CHORUS
VERSE THREE
Akuti Akufuna chikondi cha Classic
Watopa ku user zingini za Plastic
She dont wanna Compromise her quality (hehe)
Because she's Sexy and she knows it
People asking, Chikwati Chiliko liti
December Fanz ipange profit (haha)
Umangotero Chaka ndicho chiti?
Am like, zimenezo GOD knows it!
CHORUS
BRIDGE
Tsegula Khomo Amjiba alowe ey
Amjiba Afika,, Iwe
Tsegula Khomo amjiba aloweeh
Amjiba afika..
*repeat chorus then ends*
..thanks for your usual support