10146Downloads
Blakjak Che-Kalonda - Dr Che [Prod. Desert Eagle & Sispence]
Click here to download this song >> Desktop | Mobile
Mmh
Current situation.. Yeah man.. you
Blakjak Indee.... you
Desert Eagle, Sispence
Akazi Akufuna Dr. Che
Whaaaaayahsayyy
Indee...
Chorus
Ati.. Ati Sakufeela bho
Akumva fever Komanso Malungo
Nde Akufuna Dr. Che Am'baye
Dr. Che Am'baye x2
Verse One
(Eyoh Eagle) Anabwera Kwathu dzulo
Kufikila kulowa Ndili mtulo
Kenako Nkudzakoka Ka Pillow
Mmnh, Basi pompo tulo
Mmwawa Podzuka Akukhetsa msonzi
Zatheka Bwanji kuti zifike Chonchi
Thupi latenthelatu ngati Patient
Oooh God! Latentha ngati patient
Verse Two
Ati Wadwala Akufuna achile
Wakhalira Kugona Akufuna Ayime
Adye zipatso komanso Avine
Mwezi uwale tisewere Tiimbee
Komatuuuu,, Siine doctor poti
Nkakubaya poyipa sulira Moti
Ati Nzabhobho Kuyankha Mwakhonfii
Mmmmm Akuchita Kuyankha Mwakhonfii
Verse Three
Panopa Nkhani yashupha
Ndikungoyenda modumphadumpha
Ndinamm'baya nde Watupa
Angotulukanso Thukuta
Apa nditani Ase
Akazi Onse angofuna Dr. Che
Komatu Ine ndilibe licence
Nditha ndine Nzanu Sispence
Chorus
Outro