23580Downloads
Tsar Leo - Misonzi ft Teddy (Prod. Ckay & Mwanie)
Click here to download this song >> Desktop | Mobile
Baby Mtima wanga unautenga
Ndipo mzimu wanga unavomera
Ndisaname unkandipatsachimwemwe eh
There was only you, ndimapanga za iwe
Mami Mami unandiswera Mtima wanga
Mami mami utandibera Mtima wanga
I was convinced kuti ndapeza
Mtima wanga wadekha.
Hook
Nkhani ya chikondi?
Imandigwetsa nsonzi
Kapena mwina ndi ngozi?
Unandisiya chonchi?
Unandisiya Misonzi x4
Verse 2
Mesa unkandikonda?
Ine ndinkakukonda baby
Ife tinkakondana , atleast that's what I thought
Oh baby
How did we end up here eh?
Olo unandisaya bae ,Ndinkakukonda x2
Panopa nkhani ya chikondi?
Imandigwetsa nsonzi
Kapena mwina ndi ngozi?
Unandisiya chonchi?
Unandisiya Misonzi x4
Bridge
Unandisya Misonzi x 8
Hook
Nkhani ya chikondi?
Imandigwetsa nsonzi
Kapena mwina ndi ngozi?
Unandisiya chonchi?
Unandisiya Misonzi x4