4474Downloads
IKK - Fire (Feat. Bucci) (Prod by Don Foxxy)
Click here to download this song >> Desktop | Mobile
Kodi ndiwe ndani lako dzina/
Tiye pa Dance floor pang’ono Tingovina/
Chilichonse ukufuna panopa uzimwa/
Munthu olungama pa iwe atha kuchimwa
Thupi lako, mbina yako zili nyatwa
Opanda Dora pa iwe sanga peze mpata
Mtima wanga pa iwe wangomata
Ine njale iweyo yanga starter
Uli steel ngati mac siuzatha
Ndiwe Ndiku Diwa pano Ndikuthatha
Information ya Dora Zanga uzisunga Data
Kubwera kwako mumtima mwanga muli bata
Kulikonse pa mbuyo ndizikusata
Osasiyana nawe ngati thabwa ndi lata
Auze makape pano uli m’manja mwa shata
Osati Rasta ndati shata
Hook (BUCCI)
Babe thupi lakolo fire!
Kankhope kako fire!
Wabukisa moto fire!
Ndakakanika kuzimitsa owo oooH!
Ndipanga za iwe basi fire to fire
Iwe! Fire to fire*2
Ndipanga za iwe basi moto ku moto
Iwe! Moto ku moto*2
Verse 2 (BUCCI)
Oooh girl you got my attention
Somethinh I can turn away from
Look how you got my heart… my heart brazing, burning fire fire
Ndanjenjemera wandipasa ma filu ine phuma uuuuuuuuuuuuuuu!
Wamatilira game ndiyako wamangilira
Palibe omaka palibe omaka
No ooo ooo aaa
Wamangilira game ndiyako wamatilira palibe omaka paaa liiiiiiiibeeee……………
Hook (BUCCI)
Verse 3 (IKK)
Kodi kwanu mkuti
Ndaombera kare ndiwe mufti
Alipo kale kapena uli wekha
Change banja ndiwe sindidekha
Kungomwetulira paden ndikutenga
Dora number one ndiwe ndapenga
Iweyo first hustle yanga izibwera second
Kuti timange banja tasala ndima seconds
Ndukaikanso ngati uli ndi matenda
M’mene ulili mwaiwe sangalowe matenda
Owatumizayo Back to sender
Ndikuphunitsa fast poti ndiwe Bomba
Iwe siogwidwa ndima celeb ake ma zoba
Ungolenga misala zomba
Ukakakhala munyanja bwezi uli uyo
Dora, yakoma, yosowa nsomba
Hook (BUCCI)