Ritaa - Kuwawa ft Piksy (Prod. Sispence)
Name of album : Kuwawa Genre :Afrobeat
Thumbnail

Click here to download this song >> Desktop | Mobile


[Chorus]
Ukundiiwala, nde chikondi chikuwawa
Chikondi chikuwawa
Chikondi chikuwawa. Eh
Ukundiiwala, nde mtima ukuwawa
Mtima ukuwawa
Mtima ukuwawa. Eh

(Verse 1 , Ritaa)
Kunjaku kwacha, tili pompaja
Milandu yanji yosatha? Oh oh oh
Unasiya kunditchula
Timaina tachokondi tija
Kodi waponda mwala?
Zoti uli ndi mkazi pano waiwala
Sumandilabadila, mwina Wapeza wina
Ndayamba kukaikila, kuti udzandisiya
Mtima ukuwawa
Mtima ukuwawa
Zikundivuta ndafuna kumvetsetsa
Koma ndalephera

(Chorus)
Ukundiiwala nde Chikondi chikuwawa
Chikondi chikuwawa
Chikondi chikuwawa. Eh
Ukundiiwala nde mtima ukuwawa
Mtima ukuwawa
Mtima ukuwawa. Eh

(Verse 2, Piksy)
I’ve been stressed lately, work mainly
Zonse Zili bho, Chikondi still stately
I appreciate that you respect me
Chikondi chiyambiranso being tasty
Iam sorry I let you down,
Every week am out of town
Babe I’m working, but thanks for checking
Ndipanga zotheka kuti zonse zitheke
Iam the luckiest man in the world,
Ndi iwe pambalipa I can never fail
Ndiwe mkazi Wakumwamba I can tell,
Nde usamadandaule you’re my girl.

(Chorus)
Ukundiiwala nde, Chikondi chikuwawa
Chikondi chikuwawa
Chikondi chikuwawa. Eh
Ukundiiwala nde, mtima ukuwawa
Mtima ukuwawa, mtima ukuwawa. Eh

Ndili ndi mantha,
ndingadzagende Katauluka.
Oh no, oh no...
Ndiwe wekha, sukubetsa
Umabebetsa sakugwetsa
Akulenga, sakuvencha
Ndine chips, iwe ndiiwe Ketchup

(Chorus)