2069Downloads
Climax - Opanda Amayi (Prod. W Entertainment)
Click here to download this song >> Desktop | Mobile
Lyrics)-2020
Intro
Palibe chowawa ngati kukhala opanda Mayi!!(Conqueror!! Conqueror!! ))//
Moyo umawawa ngati ulibe Amayi!!! (Climax to the max)//
Moyo unakhala bwanji? ×2
Verse 1
Aaa! Life imakhala simple akakhala moyo Makolowa//
Koma Ama akapita kumasowa Kholowa//
Umayamba kutolatola ngati Mbalame//
Step mother ndikuzachotsa ku Academy//
Umalephela kugwila remote mene ukagwilila earlier//
umatha kuchoka ku Urban to Remote area//
Ndee!! akakukana Uncle//
Umachita kusowa okugwila Ankle//
Ana akulila.. Akulila!! (Akulila!!!!!! )//
Palibe owa samalila!!!!!
Hook
Palibe Chowawa ngati kukhala Opanda Mayi( Opanda Mayi!! )//
Moyo umawawa ngati Ulibe Amayi( Ulibe Amayi!!!)//
Moyo unakhala bwanji?( Moyo!! Moyo!!)
Moyo unakhala bwanji?( Moyo!! Moyo!!)//
Nanga tidzikhala bwanji?(tidzikhala bwanji??!!... Motherless)
Verse 2
Tikhala bwanji?
Amami apita!!(aaa!!)//
Tikhala bwanji?
Adad apita!!(aaa!!! )//
Tikhala bwanji?
Azakhali apita!!(oono!! )//
Tikhala bwanji?
Malume apita!!!(onoo!!! )//
Ine ndimadabwa!! Wina akamanyoza amama(Why Why Why)//
Ine ndimadabwa!! Wina akamaphweketsa amama(Why Why Why)//
Mwina samadziwa mene uwawila Umasiye//
Mwina samadziwa!! mene uwawila Umasiye!!
Hook × 2
Palibe Chowawa ngati kukhala Opanda Mayi( Opanda Mayi!! )//
Moyo umawawa ngati Ulibe Amayi( Ulibe Amayi!!!)//
Moyo unakhala bwanji?( Moyo!! Moyo!!)
Moyo unakhala bwanji?( Moyo!! Moyo!!)//
Nanga tidzikhala bwanji?(tidzikhala bwanji??!!... Motherless)
@Conqueror music group