JEG Tellem - Yekha (Prod. DJ OK)
Name of album : Yekha Genre :Afrobeat
Thumbnail

Click here to download this song >> Desktop | Mobile


ye ye yeee
yeeeh
oh Yeeeh Tellem
aha Yeah here we go

Ndimafunitsitsa nditakhala wabwino
Aliyense atamatengela ine
Ndimafunitsitsa nditakhala chitsanzo
Cholozeka pagulu la anthu
Koma nthawi zambiri
Ndimagwetsedwa Mphwayi
Chifukwa Cha zinthu zondizungulila
Ndati nthawi zambiri
Ndimabwezedwa mbuyo Chifukwa Cha zochita za anthu ena

Moyo wanga aha
Njira zanga izi
Ndimafuna zizikhala za Yehova yekha
Thupi langa aha
Ntchito zanga izi
Ndimafuna ndizichita za Yehova yekha
Moyo wanga aha
Njira zanga izi
Ndimafuna zizikhala za Yehova yekha
Thupi langa aha
Ntchito zanga izi (Izi)
Ndimafuna ndizichita za Yehova yekha

Ndimafuna
Njira zanga utasintha
Ndimafuna
Koma zimandikanika
Ndimafuna
Ndimafuna kukomana
Ndimamuna
Mamuna wa mtanda koma
Koma ndikazamva za abusa
Awapezelela ndi sister
NKHANI ija ayiphiphilitsa
Ine sizimandilimbikitsa ehe
Ndikaona zophinja
Sindichedwa ine kugiva
Sindisilila u beliver
Ndimaona ngati ndichedwa ehe

Moyo wanga aha
Njira zanga izi
Ndimafuna zizikhala za Yehova yekha
Thupi langa aha
Ntchito zanga izi
Ndimafuna ndizichita za Yehova yekha
Moyo wanga aha
Njira zanga izi
Ndimafuna zizikhala za Yehova yekha
Thupi langa aha
Ntchito zanga izi
Ndimafuna ndizichita za Yehova yekha

Moyo wanga aha
Njira zanga izi
za Yehova yekha
Thupi langa aha
Ntchito zanga izi za Yehova yekha

Za Yehova yekha za Yehova yekha
Zizikhala za Yehova yekha
Za Yehova yekha za Yehova yekha
Iye Yesu