Hustle Gang - Bwanji Umakana
Name of album : Singles Genre :Dancehall
Thumbnail

Click here to download this song >> Desktop | Mobile


(Intro by Thews P)
Mmmm hustle gang
Ndi one
Aaaaa
Mmmmmm

(Hook)
Bwanji iwe umakanayi
Kuti mkaziyu siwako iwe!
Nanga iwe umakana yi
Kuti sunapeleke mimba iwe!
bwanji iwe umakana yi
Kuti mkaziyu siwako uyu!
Pano ndiye ukukana
Ukuti mwanayi siwako!

(Verse 1 by Benja)
Dzana lija man munazitenga ngati shasha
Mutafunsidwa za mimba mutaikana
Lero lino bhasi nkhani yaphulika yokha
Zadziwika ndinu mimba mwanayu munamupasa
Mhh,,ndimwanayu mukufanana
Nanga bwanji mukumkana apayi?
Mukalimbika kukanaku
Ndisaname man ine pano ndikukhapani!
Mmmmm

(Hook)

(Verse 2 by Thews P)
Umangotinamiza kuti ulibe wina yi
Koma kumbali ukupanga zina ndi zinayi
makolo ake pano nde akuvutisayi
Akunena kuti ndiwe amene wamutupisayi
Kodi khalidwe lako ndilotani
Umangofuna kumuonongera ma plan
Bwenzi iyeyo atapangatu zina
Anthu pano
Akanamutchatu makhumutcha
Mmmmh

(Hook)

(Verse 3 by King g)
Bwanji umakana kuti mkaziyu siwako!
Koma mtima kuzunza
Mtima kuzunza
Man mulibe chilungamo
Chabwino ndakumvesa kuti kaziyu siwako
Koma tawona mfanayu
Chipumi ukufanana
Taona mfanayu matewe ukufanana
Koma sizitheka kuti mkaziyu umusiye!