29353Downloads
Blaze - Mtima (Prod. Jay Emm)
Click here to download this song >> Desktop | Mobile
Lero ikhala finals
Undiuze umaona chani mwa ineyo
Ukamanditreater chonchi
Umati ndine ndani kwa iweyo
Kodi mesa amati m`modzi mwa ifeyo
Anachokera kunthiti ya nzache
Ndikudabwa kuti m`modzi mwa ifeyo
Salabadira mkomwe zanzache
Bridge
Zizikomera mbuzi kugunda galu chikondi chanji darling
Kukhumudwitsa nthiti mtima uli m`malo umakwanitsa bwanji darling
Chorus
Kukonda iweyo, sikuti ndikupusa ayi
Ndikamakupepesa, sikuti kusatira khusa zako
Koma mtimaaa,
mtima wathu uzatipusitsa ife
Abale chikondiii,
chikondi chathu chizatipwetekesa ife
Tisafele mphathi
Verse 2
Ayi ndisaname sweet inu,
inu mwanditora pamudzi pano
Ngati kuti mwina ine ndilibe kwathu
Mwanditora pamudzi pano
Ine ndikalakwa ndimapepesa
Koma ayi mpakana suspension
Mukalakwa ndimamvetsetsa
Munthu sangalakwire mtengo
Bridge
Zizikomera mbuzi kugunda galu chikondi chanji darling
Kukhumudwitsa nthiti mtima uli m`malo umakwanitsa bwanji darling
Chorus
Kukonda iweyo, sikuti ndikupusa ayi
Ndikamakupepesa, sikuti kusatira khusa zako
Koma mtimaaa,
mtima wathu uzatipusisa ife
Abale chikondiii,
chikondi chathu chizatipwetekesa ife
Tisafele mphathi
Bridge
Usazuze mtima
Usazuze mtima
Usavulaze mtima wa ine
Usazuze mtima
Usazuze mtima
Usazuze mtima
Usavulaze mtima wa ine
Usazuze mtima
Kodi mesa amati m`modz mwa I ifeyo
Anachokera kunthiti ya nzake
Ndikudabwa kuti m`modzi mwa ifeyo
Salabadira mkomwe zanzake
Chorus
Kukonda iweyo, sikuti ndikupusa ayi
Ndikamakupepesa, sikuti kusatira khusa zako
Koma mtimaaa,
mtima wathu uzatipusisa ife
Abale chikondiii,
chikondi chathu chizatipwetekesa ife
Tisafele mphathi