123295Downloads
Piksy - Chonchobe (Prod. Don Foxxy)
Click here to download this song >> Desktop | Mobile
Foxxy i see you
Piksy
Ayeee ena adzatsalaa
VERSE ONE
Mboba osaphweketsa
Game pa mwamba osadekhetsa
Fanz yavaya utsala wekha
Ukapusa sudzawapeza
Siukudabwa akum'feela neighbor
Ndeno madolo aku pretender
Timawadziwa nde tingosetha
Kutinamiza they doing better
CHORUS
Mukumva bwanji mnthupi?
Chonchobe
Bwanji mwavala Juzi?
Chonchobe
Ma post timawaona mboba
Oh sorry
Timadziwa kuti mukunama koma
Chonchobe
Mukumva bwanji mnthupi?
Chonchobe
Bwanji mwavala Juzi?
Chonchobe
Ma post timawaona adona
Oh sorry
Timadziwa kuti mukunama koma
Chonchobe
VERSE TWO
Akuchita kuvala mbina
Awonekeko bho pa picture
Kukumana naye ndi munthu wina
Koma iyi ndi nkhani ya tsiku lina
Pa social media mboba simunama
(Ndinu bwana)
Kukhalira kunamiza atsikana
(Mumakwana)
Koma Ayeee ena adzatsala
Nokha mupeze ma ansala
CHORUS
Mukumva bwanji mnthupi?
Chonchobe
Bwanji mwavala Juzi?
Chonchobe
Ma post timawaona mboba
Oh sorry
Timadziwa kuti mukunama koma
Chonchobe
Mukumva bwanji mnthupi?
Chonchobe
Bwanji mwavala Juzi?
Chonchobe
Ma post timawaona adona
Oh sorry
Timadziwa kuti mukunama koma
Chonchobe
VERSE THREE
Kupanga tweet kutchila ndi ma dada
Ku mount soche muli pa Zode (Zodetsa)
Kutenga selfie ma chills ndi my girls
Ku Four Seasons muli pa Mbowe
Mukumva bwanji Mthupi
Chonchobe
Ayeeee ena adzatsala
Mboba osaphweketsa (ndinu bwana)
Nokha mupeze ma ansala