Stich Fray - High Grade
Name of album : High Grade Genre :Dancehall
Thumbnail

Click here to download this song >> Desktop | Mobile


Intro


Yoh x9
School ndinamaliza
Yoh X9 high grade yoh

Verse 1


Chillin pon di corner wit my buddies
Zomwe timapanga sitiwopa police
Smokin high grade all day ntchito tilibe pano kuno anthu tinatha ma plan
Yeh 
ndayesa kugulisa mpunga
Ndayesa kuyimba komabe osatchuka
Ndayesa kugulisa msomba 
kugulisa thobwa kuthamanga mpakana mpamba kudukaa
(Eeeeeeeh)
Kodi ndani anandilodza ine
Please chonde muwuzane ngat mulipo chonde muchenjezane ine ndat
(Eeeeeee)
Kodi ndani anandiloza ine now I can't walk,I can't talk, I can't jog till I smoke

HOOK


School ndinamaliza (Eeeeeeee)
Koma ntchito sikupezekaaa (Eeeeeeh)
Zibwenzi sizikuyendaa,nazo ndlama kusowa ngat tinayambana
So I smoke some high grade (Alright)
Smoke some high grade (Alright)
Smoke some high grade (Alright)
Smoke some high grade (shaaaa)
Smoke some high grade (Alright)
Smoke some high grade (Alright)
Smoke some high grade kut ma stress achokee

Verse 2


School fees ikusowa
Okoma mtima nawo akusowa
Chamba chokha ndi chimene chikupezeka 
Chikasowa ndekut upezeka ndi mowa
Ndlama nazo zikusowa
Banja nalo likusowa
Chochita nacho chikusowa
Ikakhala mphasha nayo ikusowaa
ndayesa kugulisa mpunga
Ndayesa kuyimba komabe osatchuka
Ndayesa kugulisa msomba 
kugulisa thobwa kuthamanga mpakana mpamba kudukaa
(Eeeeeeeh)
Kodi ndani anandilodza ine
Please chonde muwuzane ngat mulipo chonde muchenjezane ine ndat
(Eeeeeee)
Kodi ndani anandiloza ine now I can't walk,I can't talk, I can't jog till I smoke.

HOOK


Outro


AlrightX8 yoh haha Stich Fray on this
Eeeh high gradeX3
AlrightX8