Kabhoz - Yavuta Ndi Ndalama (Prod. Janta & Malde Beats)
Name of album : Yavuta Ndi Ndalama (EP) Genre :Hip Hop
Thumbnail

Click here to download this song >> Desktop | Mobile


HOOK!!
Pa Malawi yavuta ndi ndalama basi
Panopa yavuta ndindalama basi
Ndikuti ndindalama basi
Basi ndindalama basi! (X2)

PRE CHORUS
yavuta ndi ndalama basi
Panopa ndi ndalama basi
tikuti ndi ndalama basi
Basi ndi ndalama basi

VERSE 1
Pa Malawi yavuta ndi ndalama basi//
Utha kuyenda kwambiri koma sungatole pansi//
Kukwera bus kuona ntengo ndingosika basi//
Kuonanso mtengo wamchere apa ndingokhala lansi//
Kabaza njee bola kungoyenda pansi//

Kugulanso nyama akuchulusa mafupa//
Ine kuwafusa ati sorry mphwanga pepa//
Kagule tomatoe akuti dhilu ndikutupa

Miyambi imati time is money//
Or ndizipeze man dollars ndi zimane//
Olo nditakhala kuti ndilibe honey//
Kugula bonya bolani andikwane//

Amayi zikomo kwambiri munandilera//smunandipusise panopa ndinachenjera//
Mikoko imati waulesiyo asadye//komatu olimbikafe dzuwa likulowa tisanadye//


HOOK!!
Pa Malawi yavuta ndi ndalama basi
Panopa yavuta ndindalama basi
Ndikuti ndindalama basi
Basi ndindalama basi! (X2)

PRE CHORUS
yavuta ndi ndalama basi
Panopa ndi ndalama basi
tikuti ndi ndalama basi
Basi ndi ndalama basi

VERSE 2
Ndinali fulu anthu amandikamba//
Ati ndinatha panopa sindikumasamba//chifukwa chamakala akuti ndine mlamba//
Ndawauza yavuta ndi dola ya chakulamba//

Chick kuti ikulole imafila zidola//
Ati amafila mafana owala ngati solar//
Akazi akumalawi panonso analowa dollar(yeah pano analowa mbola)

Vuto lomwe lilipo kwa ex wanga Sarah//
pamene ndilibe dola ati sindikumushala//ndapepha reback akuti ndizamisala//
Ati ndimuleavy(ndimusiye)coz ndilibe kaisala//

Ndeno ndinacrasher ndinathoka sten yanga//
Ndinati panopa andivuta ndimafwalanga//
Kufunsa ma boss ati dollar zikutalker//
Ati popanda dollar pamalawi suutchu?kaaa//HOOK!!
Pa Malawi yavuta ndi ndalama basi
Panopa yavuta ndindalama basi
Ndikuti ndindalama basi
Basi ndindalama basi! (X2)

PRE CHORUS
yavuta ndi ndalama basi
Panopa ndi ndalama basi
tikuti ndi ndalama basi
Basi ndi ndalama basi
....
Chat Conversation End
Type a message...