28708Downloads
Azizi - Nasibeko ft TruMel
Click here to download this song >> Desktop | Mobile
(Ayi ayi aii) Uwoo oh ooooh oo (A2121 MIT CROUZY & Trumel pon di place mi say) I miss you i miss you my lady
Chorus
-Alikuti Nasibeko mmangofuna ntangomuona,
- Alikuti Nasibeko mmangofuna ntangomuona
Nkhope yake yowala mm mmangofuna mtangoionaa
- Thupi lake losalalaa mmangofuna ntangomuhoda,.
(Verse1 A2121)
-Ili ndi fuso lomwe ndalandila kuchokera kundendeko
- Nkhani yomwe inamanga nthenje eh njokhudzana ndi Nasibeko,
- Mchimwene analira momwe ndinamangidwira Nasibeko osadzandionako,
-Ngati pali china chomwe ndinamulakwila mumuuze akhululukeko o
- Ine jenkha ulephera kuyankha nkamba chani za Nasibeko,
- Ndimati nkati mwina mwake nsokoneze nkhani wandifusa za Nasibeko oh,,,
(Chorus Trumel)
( Verse 2 Trumel)
- I'am deep in the dackness,
- Kukhala moyo wa madness
- am dying for your Caress
- Cyaa wait (cant wait) to see your face (Listen)
- Ndamusowa Jane ndi Junior,
Ndidziwa nao asowa ineyo,
- Ndikhala bwanji opanda iweyo,
- Poti chikondi changa ndiiweyoo,
- You don't know how much a wana get out of here,
- A wana come down dear,
- A wana see you ma dear (oo oh)
(Chorus Trumel)
- Alikuti Nasibeko mmangofuna ntangomuona,
- Alikuti Nasibeko mmangofuna ntangomuona
Nkhope yake yowala mm mmangofuna mtangoionaa
- Thupi lake losalalaa mmangofuna ntangomuhoda,.
(Verse 3 A2121)
- Iyi ndi kalata yomaliza tawelenganii yomwe adasiya Nasibeko,
- Dziko lopanda iwe nchimodzimodzi mtsinkho wa nkhwanii opanda nchere ndi Tomatoe,
- Ana awiriwa uli ku ndende mlela ndanii nkhawa idagwira Nasibeko,
- Tsalani bwino dziko lapasi lokonderalii ndatha ndine wanu Nasibeko.
- M'banda kucha wina anthu olawilira
- Anamupeza Nasibeko wadzimangilira
- Anatikuwira mudzi onse unathamangira,
- Mwatsoka tinakapeza Nasi wamwaliraa ah,
(Conclusion)
- Alikuti Nasibeko (Nasi anamwalira a)
Alikuti Nasibeko (Nasi tinakwilira a)