Thewz G - Mkazi Wanga ft Kell Kay (Prod by Henwood, Tricky Beats & Thewz Exclusive)
Name of album : Mkazi Wanga Genre :RnB
Thumbnail

Click here to download this song >> Desktop | Mobile


(Verse 1)

Hello, Mkaziwanga,
I know you know
That I love you so....
Ndipolero
Ndifuna uziwekut
Kubwela kwako mmoyomwanga
Wasintha zinthu zambili.

Bebi ndiwe Makina ,osokela love yanga..
Daling umaziwa zofooka zamtima mwanga..
Ndipo ndikulumbila
I will be with you forever..
My sweet potatoe ....oya ma bebi Oooh.

Bebi you are wonderful.
I like you body particular.
Beb ndiwe umandikweza temperature ..
( I need you to go down , ine sindiilola, mpakanakutopa.)


(Chorus)
Mkaziwanga iwe iwe iwe......
Ndakukonda ine ine ineyo...
Undipase zonse iwe iwe iweyo
Mkaziwanga iwe......

(Verse 2)
Oyeh ,,
oya ma bebi undipase zonse zofunika mchikondi...
Pokupanga appreciate nzakupasa tima luwa eeeh...
Bebi ndiweyo,
Amene ,
Ine ,
Ndinakonda ai, ndinakonda ai..

X2
Bebi you are beautiful (elelel mama)
I like your body particular
Ndiwekha umandikwanila
Baby
I know that you are feeling me too
Let me be the champion in your love
Baby.

( Verse 3)
Ndiwe... Chiphazuwachanga.
Ndiwe.... My one and only ...
Unamata mtima wanga.
Zilindiwe kut uzandikonde ine...
Mwinizithu ndinuyo Mami..
Ndinayamba mwano
kamba kainu Mami eeh..
Tiye tikondane iwe ndi ine
Mkamakhala mapemphelela iwe.....
Mkaziwanga iwe,,iweee ,,,ndakuko ine ..
inee... Undipase zonse iwe ,,, Mkaziwanga uweeeee ,,,eeeeh eeeeeeeeeeh...