Slessor - Puputa Misonzi
Name of album : Nkhani Za Ku Malawi Genre :Hip Hop
Thumbnail

Click here to download this song >> Desktop | Mobile


Puputa Misonzi Lyrics
Chorus
Iwe Puputa misonzi yako/ nthawi yako izakwana/
Iwe puputa misonzi yako/
Ambuye ali nawe cholinga/
Iwe puputa misonzi, Misonzi! MISONZI , misonzi yooo/
Verse1
Ndikudziwa umazifunsa, does God really exist? / is his existence really iust a myth?/ wayesetsa kupempera kwa nthawi yayitali/ panopa ungowona ngati ukutaya nthawi/ aja unkawanena kuti awa ndi otayika/ akunjoya ndi moyo iwe ukungovutika/ ooh
U think life is so unfair/ even worse its like nobody cares/
U Cant sleep, ur face covered in tears/
Uli ndi mantha, ur best friend is ur fear/
Kuyesetsa kulimbikira, zinthu osagwira/
Nchifukwa chake mam'mawa umadzuka okwiya/
Koma pali chimodzi chomwe iwe sukudziwa/ chimwemwe chimabwera m'mamawa nde osalira/
Chorus
Verse 2
Mavuto omwe timakumana nawo ife tsiku ndi tsiku/ amatikhwimitsa mu nzimu osati nsinkhu/ nde pena mulungu amatha kuzisiya dala/ koma sikuti amakhala abuye atiyiwala/
Anthu omwe unkawadalira anakutaya/ nakutcha bulutu kape, mphawi nde kazivaya/ koma anthu omwewo ndi amene azakutame/ ali sister please tandigayileni money/
Pamenepo iwe utayiphula zikuyenda/ ukuthandiza ana amasiye ndi amatenda/Nde chonde mukamanyoza anzanuwo muzidziwa/ mulungu si jemusi mawa ndi tsiku lina/
Chorus
Bridge
Mulungu samawona nkhope/
M'mbale wanga usatope/
I know he's got planz for u and and and u and u/