Click here to download this song >> Desktop | Mobile
Kumbire adanka nawo /
Palibe akanakhonza /
Anasiya pa dzuwa anawo
/ Anayesa ndi malodza /Ankati satana
/ Wakhala pa nsana / Kuyamba kudana
/ Kufuna kuphana Kuthana /
Nzosauzana /
Nthawi yakwana /
Buluzi wa easy chitseko cha mpana
CHORUS
Anapita ndi nyanga zomwe kumanda / Anapita ndi nyanga zomwe kumanda /
Ayo Tsoka Liyenda / Ayo Tsoka Liyenda
Bambo awa anali chikhwaya /
Ana moyo wawo sanamve kuwawa / Ku school akapita amathawa / Zinavuta ndi za nchere analawa / Yes Sanauzidwe za moyo / Anapeza bwanji makolo/Chuma/Moyo unakoma/Opanda zo khoma/Kupeza izo afuna/Ohh dzi ana ulesi/Bambo awo atsamira nkono
Akuti zonsezi /Ndi curse/Chayabwa chitedze/Mavuto pang'ono see they stressed/
CHORUS
Mudziwaphunzitsa ana/SiKupangira pa mawa/Asamayese ngati ophweka moyo/Mukadzapita adzakhala akapolo/ Musama yiwale/Kuti zanu munapanga kale/Nzeru zanu sizingatsale/Mungadzavutitse abale/Mdzakolola zomwe mudzale/Chuma ichi sangasamale/Ngati panopa simuphunzitsa/Mapangidwe ake mukumpusitsa/Tsoka ilo
CHORUS