30383Downloads
Blakjak Che-Kalonda - Ndi Inayake
Click here to download this song >> Desktop | Mobile
NDI INA YAKE LYRICS
INTRO
Blakjak- Indee! (GD)
Nthawi ina yake timazamenya ina yake umadziwa
Ndi ina yake koma eti,,, Indee! Eeh!
CHORUS
Tsiku lina lake/ Ndili pena pake
Ndili ndi wina wake/ Ndikumenya ina yake
Panadutsa wina wake/ naye ali ndi wina wake
Mmmmmh ma Man, Eeeh!/ Ndi Ina yake
Inali nthawi zanji? Unkapanga chani? Nanga zinatha bwanji? (Ndi Ina Yake)
Unali ndi ndani? Amakupanga Chani? Anakuwona ndani? (Ndi Ina Yake)
VERSE ONE
Kale kale kunali Baibe inayake
Inali Baibe ya a Frenzi athu ena ake
Tinkagwirizana Heavy udziwa munthu ndi Mlamu wake
Koma zinachitikazo mmm ndi ina yake
Anandikhola kwawo tsiku lina lake
Ati ndivaye afuna akandithoke zina zake
Nditavayako nnapezako kuli Mdala yake
Nnangonamizira kufunsa Map udziwa ina yake
After time Nnalandilanso phone yake
Ati nditha kuvaya Mdala wayendera yake
Ma Guy ambiri akuti (baibe’yo ndi ndani dzina lakee!!)
Easy, nditchula dzina mwina nyimbo ina yake
CHORUS
VERSE TWO
Tsiku lina ndikuyenda Mntauni penapake
Man anandikodola akuyitana mkazi wina wake
Ine kuvaya, nnampeza iye ali ndi nzake
Koma sinnadziwe kuti ngini yake ndi Ina yake
Boh ujeni? Ndikudabwa akugwetsa nkhope yake
Sinnadziwe uyu si ujeni,, ndi sister wake
Akuti ndi ma twins, ndangomva kwa nzake
Mmmmmm ngini yake man, ndi ina yake
Nde ndadziwa kuti uyuy ndi sister wake
Ndayamba kumfunsira wandipatsa nambala yake
Ndamuuza kuti tikumane mawa penapake
Tizamenye inayake,, udziwa,, ina yake
CHORUS
VERSE THREE
Ngini yayamba kuyenda boh yafika pa chimake
Nzanga uja ndi ujeni, ine ndi twin sister wake
Kuyenda limodzi, kuphaka life thaimu ina yake
Komano ngini inazashupha Tsiku lina lake
Nnavayanso kwawo day ina mwa mwambo wake
Anandisekelera udziwa khalidwe lake
Tinatengana yathu ija kuvaya penepake
Wandigwira-ndamugwira basitu,, inayake
Frenzo anatulukira naye ali ndi Baibe yake
Baibe’yo ikungolira itangomuwona sister wake
Akuti ndalakwitsa uyuyu ndi sister wake
Koma frenzo naye anali atamenya kale inaya yake
CHORUS- Till song ends
All rights reserved (2014-Blakjak)