Roudeezy - Ashu [Roudeezy & Jolo Justice] (Prod. Raj Records)
Name of album : Ashu Genre :Hip Hop
Thumbnail

Click here to download this song >> Desktop | Mobile


INTRO
AJolo Justice ( Roudeezy virus)
Raj Nation
Shoemaker X 3

VERSE 1
Ndabwela ndi nsapato zinayi
mundipangileko zithu zinayi
ndikavala zikumandigwesa phwayi
sindikuzifunaso munyumba yangayi
wazandimbila Foni Jolo
tandipeze ndili ndi akazi folo
mamuna ndekha ndangoyima ngati Polo
sindikusiyanisa pagolo ndi golo
ndikusoka kaye Jombo
koma ndichedwelako ili ndi zilombo
ndikufuna ndingoyizungulisa round
chifukwa ili ndi makwacha, madollar, mapounds
ndangofika angochepesa khani
tagawana two, two game ili pa mpani
nkazi nkuzandifusa iwe ndi Ashu kani
ndat eee ndimasoka chingandivute nchani

HOOK
Sindine teacher.....
kuwelenga sinditha
ku xul sinapite
sindine Dj....
kundipasa mixer
ayi singamixe
ndine Shoemaker ( Ashu...)
shomaker. ( Ashu Ashu)
ndine Shoemaker ( Ashu)
Shoemaker.( Ashu Ashu)

VERSE 2
tchito yanga ndiyomweyi
ndiyomwe ikumandipasa mwayi
bostik ndi chisongole
ndizomwe zikumapezeka mu nyumba yangayi
kodi mesa mumakonda Peza
inu Madzi mumasamba pa guyser
ndiye tingamange bwanji banja
chifukwa ife uphawi unatigwila zanja
iwe pano ukundika pa easy
mamuna wako akumandipasa busy
tchito yanga ndiyomwe ingapangise
kut khaniyi mpaka ikulisise
kaya mwina ndimayeselo
kapena tikupanga sewelo
ndiye ungavale bwanji velo
pomwe ine nkalas ndimangopexa ma zelo

HOOK
Sindine teacher.....
kuwelenga sinditha
ku xul sinapite
sine Dotolo
zakuchipatala sindiziwapo kathu
ndine Shoemaker ( Ashu...)
shomaker. ( Ashu Ashu)
ndine Shoemaker ( Ashu)
Shoemaker.( Ashu Ashu)

VERSE 3
Kodi ungandiuze zingatheke bwanji
tchito yokhala yanga yanga
akazi si anga ndi anu
ine ndimangosoka basi!!!!
Akazi ndi anu si anga
ine ndimangosoka nsapato ooh
nsapato ine ndimangosoka nsapatoooo

HOOK
Sindine teacher.....
kuwelenga sinditha
ku xul sinapite
sindine Dj....
kundipasa mixer
ayi singamixe
ndine Shoemaker ( Ashu...)
shomaker. ( Ashu Ashu)
ndine Shoemaker ( Ashu)
Shoemaker.( Ashu Ashu)

HOOK
Sindine teacher.....
kuwelenga sinditha
ku xul sinapite
sindine Dj....
kundipasa mixer
ayi singamixe
ndine Shoemaker ( Ashu...)
shomaker. ( Ashu Ashu)
ndine Shoemaker ( Ashu)
Shoemaker.( Ashu Ashu)