Click here to download this song >> Desktop | Mobile
1st Verse
monga momwe adalengela Adamu ndi Hava
ndimomwe zilili
kudikira kupilira kudutsamo muzokhoma
kwa nthawi yayitali
pano ndikuona maso mphenya
iwe ndi ine takalambitsana
tili ndi ana, ana athu ali ndi ana awo
Bridge
poti mamuna, adzasiya makolo ache
wautali, kukakhala ndi nkazi wache
nayenso nkazi, adzasiya makolo ache
wautali, kukakhala ndi mamuna wache
Hook
tsono tikudikiranji, iwe ndi ine X3
mwalo momanga banja
tikudikiranji, iwe ndi ine X3
mwalo movekana mphete
2nd Verse
i can't wait
kuti ndizakutengere kunyumba kwa Amayi ukawonekere
i can't wait
kuti Amayi ako ndi Amayi anga azakhale asewele
i can't wait
zija zomagonelana pamwendo tinkhani tikukambirana
zija zomathamangitsana mnyumba kusowetsa mtendere aneba
i can't wait
zija zomayambana mawa nkugwirizana
i can't wait
zija zoti lero kutaya chakudya mawa nkugona ndi njala
i can't wait kuti uzakhale mayi a chiyembekezo
udzadutse mu zonse Amayi amadutsamo
Bridge
mamuna, adzasiya makolo ache
wautali, kukakhala ndi nkazi wache
nayenso, nkazi adzasiya makolo ache
wautali, kukakhala ndi mamuna wache
Hook
tsono tikudikiranji iwe ndi ine X3
mwalo momanga banja
tikudikiranji iwe ndi ine X3
mwalo movekana mphete
Bridge
will you marry me? X2
i wanna make you be my wife X3
Hook Till Fade
tikudikiranji iwe ndi ine X3
mwalo momanga banja
tikudikiranji iwe ndi ine X3
mwalo movekana mphete