14308Downloads
Mary Chilima - Tikupatsani
Click here to download this song >> Desktop | Mobile
Onse ma bae anagwira konkuno, ndipo akudziwa mavuto a m'dziko muno
Njala, nthenda, usiwa, pano zili ponseponse, Ndipo chomwe tikusowa pano ndi nzeru za Mose
Atitsogolere tigwirane manja tonse, ndikuyambiranso kutukula dziko lathu lonse
Ikakhala sports osachita kutchula, mukudziwa kale kuti mpira amatha kubula
Achinyamata aluso tiiphula: ndati achinyamata aluso tiiphula!
Hook
Mukufuna ntchito tikupatsani
Mukufuna business tikupatsani
A Malawi voterani UTM
A Malawi voterani UTMmmmmm Mukufuna chitukuko tikupatsani
Mukufuna chitetezo tikupatsani
A Malawi voterani UTM
A Malawi voterani UTMmmm
5 years imeneyi taphunzira zambiri, za mmene boma lathuli liliri
Through the reforms zonse amadzitsata, koma chomwe chimasowa ndi mpata
Chomwe tipange chaka choyamba, kuthetsa katangale, kuchotsa mbava,
Kuthetsa quota system, nepotism, presidential powers tidzapanga trim
40 billion anthu a business, boma lilironse: mega farms and factories
Tikatero million jobs takwanitsa, apumbwa onse tagwetsa!
Hook
Mukufuna ntchito tikupatsani
Mukufuna business tikupatsani
A Malawi voterani UTM
A Malawi voterani UTMmmmmm
Mukufuna chitukuko tikupatsani
Mukufuna chitetezo tikupatsani
A Malawi voterani UTM
A Malawi voterani UTMmmm
Mumafuna kuti apange resign, adziulula za katangale ndani?
Akalankhula zinthu zimachitika, kuposa olalikila aja Mani!
Palibenso ena angakhonze fast, Chilima ndi Usi ndi nkhenge kumalast
Voting UTM, tsono it’s a must, for chitukuko choti chidzapanga last
Pa 21 May, vote kapange cast, osalubwalubwa just put us to the test Enawa ndi mafana kachongeni the best, SKC ndi deal, he puts Malawi first
Achinyamata, takhulupira, tsogolo lathu lafika!
Hook
Mukufuna ntchito tikupatsani
Mukufuna business tikupatsani
A Malawi voterani UTM
A Malawi voterani UTMmmmmm
Mukufuna chitukuko tikupatsani
Mukufuna chitetezo tikupatsani
A Malawi voterani UTM
A Malawi voterani UTMmmm