Click here to download this song >> Desktop | Mobile
Verse 1
ngati ulibe skinny jeans iwenso nde kaya
ngati umabwela ku den basi kazivaya
sindinyengelela bebi ine ndi one wire
pokha pokha ngati mwina umayimba choir
yemwe alibe skinny jeans ndi mkazi wa chimidzi
fungo lake mkamwa kukhala ngati la chiphwisi
zija zodya mpunga pa nthawi ya khirismis
kamwa langa si sunga zinthu za chisinsi
umandipeza poti si uvala za make dzana
makamaka zija zomwe unavala dzana
ndikukakamila mpaka ndikupase mwana
buluzi wa pa easy, chiseko china m'mpana
ur my range lover every time you bend over
r u ready 2 tell ur boy "the game over"?
awa si masamu sizofunika ku sova
ndiku gogodela ngati a mboni za yehova
Chorus
Umandipeza ukathinisa ndi skinny jeans
uzalola ndizakufusila by any means
ndi ka skinny jeans * 2
Umandiwaza ukathinisa ndi skinny jeans
uzalola ndizakufusila by any means
ndi ka skinny jeans * 2
Verse 2
skinny jeans make me look like bad like bad spencer
yandi pangisa ku gwila bebi ku deni ya a neba
usiku ose osagona june bad weather
magesi akangoti azima, time 2 go further
shes malawian but looking like american
the way she dresses cool nanga these ladies can
ka kiss kake ndi kokoma ngati sugar cane
kandi pangitsa kusamba madzi amu water can
my sweet sixteen skin' jeans size fifteen
zilibe kanthu wether ur too fat or too skinn'
ukangodutsa fanzi imayamba sweating
usiko wonse baby tikhalila texting
u be the mother of my kids, i'll be the daddy
chimakoma chilichonse ungaphike
kuvala kwake ngati ulendo waku party
mu skinny jeans pa 1 mpaka pa sate
Chorus
Umandipeza ukathinisa ndi skinny jeans
uzalola ndizakufusila by any means
ndi ka skinny jeans * 2
Umandiwaza ukathinisa ndi skinny jeans
uzalola ndizakufusila by any means
ndi ka skinny jeans * 2
Verse 3
Nkhani ili nkamwa pano ndi ya skinny jeans
akangoti wasamba samba ndimu skinny jeans
ka mini skirt katha fasho koma skinny jeans
skinny thong, skinny short, everything skinny
skinny jeans paliponse ngati hule spana
ka house girl koma so ti ana ta mabwana
too late ukamazaziwa uta pana
umazitenga ngati dolo iwe umanama
mu skinny jeans pa stereo nkhani sawasawa
ma bebi wa usayese abwelela bawa
amafuna wodula komasa osawawa
iwe kungo gula umodzi kenako kuthawa
phazi thandizeko awa tiwonana mawa
amabwela okha ngati madzi ku chikwawa
alibe ulemo, amadutsa olo kuti wawa
nkhani ya ma bebi pa malawi ndi kawawa
Chorus
Umandipeza ukathinisa ndi skinny jeans
uzalola ndizakufusila by any means
ndi ka skinny jeans * 2
Umandiwaza ukathinisa ndi skinny jeans
uzalola ndizakufusila by any means
ndi ka skinny jeans * 2