Macelba - Chisankho ft Saint & Lulu (Prod. Janta)
Name of album : Chisankho Genre :Hip Hop
Thumbnail

Click here to download this song >> Desktop | Mobile


Intro
Yeah, Look

Verse 1 (Macelba)

Unawina mtima wanga ndiwe boma/
Chikondi chakwela nde sitingatsutse boma/
Inu nde a chair kulamulira boma /
Mamie muimanso silingaluze boma/

Mamie muli ndi mtima wachikondi /
Olo ndilakwitse muli ndi mtima wachisoni/
Makutu m’natseka muli ndi mtima wachigonthi/
Siinu a njilu mulibe mtima wachizondi/

Ndinene tchutchutchu olo atsine khutu /
Sindimva za munthu kapena ndi juju/
Mtima wanga za inu unachongelatu/
Ndabwera ndabwera apapa ndafikiratu/

Chorus (Saint)
Mamie iwee ndasankha (no regret )
Mamie iwee ndasankha (there is no recount)
oh wina basi no wina
Palibeso wina ndiwe Owina
Oh wina basi no wina
Palibenso wina
Ndiwe owina

Verse 2 (LuLu)
Nthawi yomwetulila nchimake/
Mtunda watha ngati owina uli ndi ine/

Mamie chonde chilemekeZe chikondi mammie/
Mumtima mwanga ndakudulila ka munda mammie/

Zili ndi iwe kulima tiligu ndizokondwela mammie/
Zili ndi iwe kulima nansongole ndizilila/

Chorus (Saint)
Mamie iwee ndasankha (no regret )
Mamie iwee ndasankha (there is no recount)
oh wina basi no wina
Palibeso wina ndiwe Owina
Oh wina basi no wina
Palibenso wina
Ndiwe owina

Verse 3 (Macelba)

Ndikamaseka umaseka nane /
Ukamalira mtima umasweka nane/
Nazelezeka nawe wabaizika nane /
Mmene umandikondera ndimakukonda nane/

Owina owina/
Wamuntima mwanga ndiwe no wina/
Owina owina/
wamuntima mwanga ndiwe no wina/

Chorus (Saint)
Mamie iwee ndasankha (no regret )
Mamie iwee ndasankha (there is no recount)
oh wina basi no wina
Palibeso wina ndiwe Owina
Oh wina basi no wina
Palibenso wina
Ndiwe owina