3Downloads
Phyzix - Pepusa
Click here to download this song >> Desktop | Mobile
*(INTRO)*
Sameface on the beat
{Mphungu Screech sounds}
It’s Only Entertainment
*(HOOK)*
Muwauze kuti mbali zakuno sitipanga nawo za chibwana/ Pepusa Nje!
Muwauzitse kuti mbali zakunoko kudelera utupikana/ Pepusa Nje!
Kuno timakhafa/ Pepusa Nje!
Ndipo tili tougher/ Pepusa Nje!
Kuno timakhafa/ Pepusa Nje!
Ndipo tili tougher/ Pepusa Nje!
*(VERSE 1)*
Kundifusa dzina langa ndi kupusa/ alipo yemwe samandidziwa ine Pepusa?/ kundilipilitsa pakhomo ma bouncer/ muuzane kuti imeneyo ndi Pepusa/ Mafana ambiriwa ndi ma Medusa/ makhalidwe ngati njoka akaona khusa/ chomwe amabwelera ndikukuuser ine nde ndine Gangsta sindilora Pepusa/ osandiitana ku show ya dollar yopelewera/ ine ndikafika ku show nde ndimapemelera/ ndine mfana oti ndimakonda kudyelera/ ndimakonda kumwelera ndimadana ndi Pepusa
*(HOOK)*
Muwauze kuti mbali zakuno sitipanga nawo za chibwana/ Pepusa Nje!
Muwauzitse kuti mbali zakunoko kudelera utupikana/ Pepusa Nje!
Kuno timakhafa/ Pepusa Nje!
Ndipo tili tougher/ Pepusa Nje!
Kuno timakhafa/ Pepusa Nje!
Ndipo tili tougher/ Pepusa Nje!
*(VERSE 2)*
Kundiponda sneaker ndekuti timenyanapo/ ngati wamaliza kudya pa tebulo wadyapo/ ine ndine Gamba equivalent El Chapo kumuva mwa u Gangsta zonse tinachitapo/ I demand respect sindifuna za Pepusa/ ndikati ndatchena ngati chimfana cha ku USA/ wina ndikumati za TZ/ Pepusa/ pano ndineneletu ndimadana nzopusa/.. kufuna kudya chimwana ndikudya ndi Pepusa/ kunena kuti Phyzo anatha Pepusa/ ndacharger 10mita wapita ndi 1mita umafuna kundipanga undercut Pepusa
*(HOOK)* x2
Muwauze kuti mbali zakuno sitipanga nawo za chibwana/ Pepusa Nje!
Muwauzitse kuti mbali zakunoko kudelera utupikana/ Pepusa Nje!
Kuno timakhafa/ Pepusa Nje!
Ndipo tili tougher/ Pepusa Nje!
Kuno timakhafa/ Pepusa Nje!
Ndipo tili tougher/ Pepusa Nje!
Stich Fray on the board.


