377Downloads
Mr Mzaliwa - Objection ( Prod. Dry B & Stevo Beats)
Click here to download this song >> Desktop | Mobile
Mmmm Mr ayaya
Ndakupatsa zanga zonse
Undisamalire mmmm
Undichengetere eeh
VERSE 1
Taonani hunie komwe ifeo tachoka /
Analipo ambiri sankadziwa lero tizafika /
Bae you my sunshine /
I see the future /
Ndiwe moyo wanga basi “Basi!!!” /
Tenga zanga zonse basi “Basi!!!” /
Sindifuna kulira kusweka mtima ndinadutsamo /
Sindifuna kukhala ngati makoko amango /
Kunditaya palipose /
Kundisiya palipose /
Wina azachileka /
Wina azandisimba /
HOOK
Ukazandisiya /
Opanda notice ngati nyumba ya rent /
……[kaya!!!]….
Summon kundidulira /
Kulikonse kundipitira /
Sindizayimva /
Ndizapita ku court kukatenga objection /
Sindizalora /
Ndizapita ku court kukatenga objection /
Pazamfa zungu pano /
“mbambadi!!”
Pazatelera ndati /
“mbambadi!!”
Ine ndizapita ku court kukatenga objection /
VERSE 2
You promise to be the best person /
Am gonna be now good enough /
Ndapeleka nkhoza la mkuwa /
Likhale chikole /
Chikondi chokoma ngati ichi ndi machisowa /
Usakhale aja /
Anandipaka-paka matope /
Kunditaya palipose /
Kundisiya palipose /
Wina azachileka /
Wina azandisimba /HOOK
Ukazandisiya /
Opanda notice ngati nyumba ya rent /
……[kaya!!!]….
Summon kundidulira /
Kulikonse kundipitira /
Sindizayimva /
Ndizapita ku court kukatenga objection /
Sindizalora /
Ndizapita ku court kukatenga objection /
HOOK
Ukazandisiya /
Opanda notice ngati nyumba ya rent /
……[kaya!!!]….
Summon kundidulira /
Kulikonse kundipitira /
Sindizayimva /
Ndizapita ku court kukatenga objection /
Sindizalora /
Ndizapita ku court kukatenga objection /
Pazamfa zungu pano /
“mbambadi!!”
Pazatelera ndati /
“mbambadi!!”
Ine ndizapita ku court kukatenga objection /