KYC Nyimbo - Machesi (prod. Malde beats & Red Disc Music)
Name of album : Singles Genre :Hip Hop
Thumbnail

Click here to download this song >> Desktop | Mobile


MACHESI LYRICS

VERSE 1

Geli ndinamaliza timapepala ndili nato/
Inde school siimatha koma tilipobe tingapo/
Toti nkanati ndili ku dziko lina lakutali/
Tikanagwira ntchito koma osati ku Malawi/
Mdala vep inaima, ndi steniso divorce/
Pano anabalalika sitimashala limodzi/
Its been a couple of years now since I heard his voice/
Ndango-ganiza zongoiwala ndilibe choice/
My life is on fire, palibe ondiphula/
Singagweso mchikondi akazi aku Malawi anadula/
Ghetto yut alibe kwacha, akazi amamuthawa/
Akasangalala ndekuti wamwa ka bawa/
Chifukwa chomwe navaira ku geli sinduchiona/
Ndipanga bwanji inspire ana omwe akundiona/
Nde after kuboweka, ndinapanga chisankho/
Pano ndimangoyaka poti dziko ndila tsankho/

BRIDGE

Nde zikangopezeka zi dollar, ndimangoganiza zongoyaka ngati machesi/
Kundipeza ku den kwathu mbola, bola komwe fanz ikuyaka ngati machesi/

CHORUS

Utha kundiyatsira mogo ndine machesi/
Utha kundiyatsira m`bongo ndine machesi/
Ukandipeza ku nkalabongo ndine machesi/
Mechesi, machesi, machesi

VERSE 2

Kukhala ku Malawi, ndikulimba mtima /
Kuli anthu ikutha week osaona mbamu ya nsima/
Sindili pa ufulu ngati nthumba mulibe dollar/
Dollar za msonkho wanga wina chikwama anachitora/
Regimes do change but, things dont change /
Ndimakhala ozizidwa ndi nkhanizi ngati sangie/
Am 25 I should `ve been driving my own range - rover/
I got papers koma ndine lova/
Pepani atsikana lero mbina sizisuntha/
Ndiimbe zoti mukamva ubongo wanu ukhuta/
chifukwa cha umphwawi akazi analowa mbola /
utha kulandidwa lero dzulo utapheya lobola/
zimachitikazi zimandizunguza bongo/
mkona nkhawa zanga zimathera ku nkalabongo/
mfana wa degree, akungomwa nkalabongo/
after 2 years wa degree wadiwa ndi nkalabongo

BRIDGE

Nde zikangopezeka zi dollar, ndimangoganiza zongoyaka ngati machesi/
Kundipeza ku den kwathu mbola, bola komwe fanz ikuyaka ngati machesi/

CHORUS

Utha kundiyatsira mogo ndine machesi/
Utha kundiyatsira m`bongo ndine machesi/
Ukandipeza ku nkalabongo ndine machesi/
Mechesi, machesi, machesi