Saint & Macelba - Tchekela (Tricky Beatz & Sispence)
Name of album : Tchekela Genre :Fusion
Thumbnail

Click here to download this song >> Desktop | Mobile


Intro:
We here
Ine eeh, ah ah
Ine eeh, ah ah
Maluzi ziii, (musiye mzako) ah ah
Maluzi ziii, (musiye mzako) ah ah

Verse one: (Saint)

Munthu wandalama kuitana okukonda ambiri
Mpaka dollar akudyere kenako akuipitsire mbiri
Nde maluzi akapweteka
Amzako onse chekacheka
Abaleso sapezeka
Pakamwa pawo adacheteka
Ukatha ma plan
Ngati udye makatani
Maluzi ndi chipani
Choyambitsa udani
Ineee.

Chorus:
Aah Ine ine yah
Ndatchekela Maluzi ndalephela (ah)
Aah ine ine yah
Ndatchekela maluzi ndalephela (ah ah)
Ndangosanduka wolira
Ndatchekela maluzi ndalephela (ah ah)
Ndatchekela maluzi ndalephela (ah ah)
Ndangosanduka okanda
Ndatchekela maluzi ndalephela (ah ah)
Eeh ndalephela

Vers 2 (Macelba)

We here
Kuyesesa kusaka ndalama
Titole chikwama titule minyama
Kuyesesa kuthesa ulova
poti zikamavuta palibe akutchova
Kuthamangathamanga daily
Koma mavuto angochuluka daily
Mpaka pa line angondikamba
Ndichite bwanji kuti ndipeze mpamba
Wangongole afuna zake
Mkazi wapakira zake ati apita kwa make
Mwina ndiyese mtera
kapena ndilowe kuba
Kukhesa thukuta
koma maluzi sakumva ine

BACK TO CHORUS

Bridge:

(Macelba) Musiye mzako ×8

(Saint) mmmh ine eh eh
Maluzi ah ah
Ine.. mayo mayo.

BACK TO CHORUS.

Outro
(Saint)

Ndalephela, ndalephela aaah ah ah ×4