Noxien DeSaw - Akunamizana Kuti Ndiotchuka
Name of album : Akunamizana Kuti Ndiotchuka Genre :Hip Hop
Thumbnail

Click here to download this song >> Desktop | Mobile


Akangomveka pa radio mayii taputa nkhondo
Ukangoyesa kuyamikira ndiye wapalamula,
Kuchoka day imeneyo chilichonse ungankambe sazakumva
Akuti anafikapo atchuka moti akuzimva
Mudzipatsiranji umphawi moyo umafunika kulimbikira
Kumalephera kulima kumati ine mzikaimba
Munakakhala a dziko lina tinakati tsiku lina mwina
Koma as long as muli ku Malawi aman mudzavutika
Ayi please guys musakhale osalira
Anatukuka ndi nyimbo am telling you ndi anthu olimbikira
Amathamanga ndi sound, kwinaku ntchito nkumagwira
' fukwa amadziwa kuti kusiya vepi zinthu ziaipira
Umamopa mmalawi azikunyoza eti? samagonja
Atakunyoza zaka 50 iye sadzatopa
Akupezera chifukwa mpaka iwe kufooka
Nkakhala ine mmangoti kambani zanu mudzatopa nokha.
Nanga kungachele ife Tima spita ma bars,
Hah! osakamba nkhani zina bwanji?


Chorus

Akunamizana kuti ndiotchuka -
Eeh tinawamvapo daily amativuta
Kumadzipopa kumati ife ndi a nthutha -
Inde amatama koma alibe khusa -
Ndinawaudza kuno ndi kumalawi -
Iwo amadziika mu levels ya ma rappers a ku USA
Nanga bwanji pa DFB samafika?
iih sinanga ndi la ma rappers ongolira ndi mtima. (Pepani)


Ati ndiotchuka kuwapasa moni satiyankha
Tikaapanga 'Hi' pa Instagram sapanga reply
Ati ndipatali sangacheze ni munthu wamba
Takumvani ndinu otchuka koma mulibe ndalama
Mukakhala kumbali kodi mmadziika m'gulu ndani?
Musamazizunze choncho palibe amene akukudziwani
Ndinu Tecno man musamazimve u iPad
Anthu Adzalephera kukuthandizani chifukwa chamakani
Mumayankhula mwamatama komanso mwauchitsiru
Kumati ife ndiye tinablower nanga inu?
Ku blower Kwa ku Malawi man ah sidilu
Umadzikakamiza kumazipopa ukudya mpiru
Mpaka kulephera kulimbikira nazo ntchito kuopa aoneka kupusa
Nyimbo zake ziti zomwe mukuzivutitsira?
Zoti kugula CD yake lero mmawa mkukaikwilira
Two three days timva kuti oyimba uja wafwifwa

Chorus

Akunamizana kuti ndiotchuka -
Eeh tinawamvapo daily amativuta
Kumadzipopa kumati ife ndi a nthutha -
Inde amatama koma alibe khusa -
Ndinawaudza kuno ndi kumalawi -
Iwo amadziika mu levels ya ma rappers a ku USA
Nanga bwanji pa DFB samafika?
iih sinanga ndi la ma rappers ongolira ndi mtima. (Pepani)
Amazipopa kumati iwo ndiye anafikapo
Pati? Ine nkulephera kuonapo
Pezani dollar kaye man kenako muzizipopa
Maumboni azikhala anthu osati inu nokha
Kumangothoka zopanda umboni kodi simutopa?
Kapena m'makamba za ku maloto zoti sitidziona
Just wait, tidzanene ndife kuti mwa blower
Koma ngati simudzasintha tidzati ndiye mukubhowa
Ndiye mumadziwa munthu obhowa kuti timamutrani ah?
Mmmm mm mm
(Kwathuku)
Timamukhoma,
Nkuzamumenyesa ku khopa.
Kumanso kudzamuponda,
Akalimbikira kukula mtima ndithu adzadziona

Chorus
Akunamizana kuti ndiotchuka -
Eeh tinawamvapo daily amativuta
Kumadzipopa kumati ife ndi a nthutha -
Inde amatama koma alibe khusa -
Ndinawaudza kuno ndi kumalawi -
Iwo amadziika mu levels ya ma rappers a ku USA
Nanga bwanji pa DFB samafika?
iih sinanga ndi la ma rappers ongolira ndi mtima. (Pepani)