15988Downloads
Blaze - Kwabooka (Cashgate Riddim) - Blaze & Chizzy
Click here to download this song >> Desktop | Mobile
Mwatenga ndalama zonse mwaika mthumbamwanumo-
~Kwabooka kuboma kwabooka uko!
Mwina kapena mukuti tizikadya kwanuko
~Kwabooka kuboma kwabooka uko
Mitima yanu bwanji kudzikonda chonchi nanga
~Kwabooka kuboma kwabooka uko
Mesa munkati ndinu atsogoleri a dziko
~Kwabooka kuboma kwabooka uko...