Mascot - Macholowe
Name of album : G.L.C (Good Luck Charm) Mixtape Part 2 Genre :Hip Hop
Thumbnail

Click here to download this song >> Desktop | Mobile

Intro
(This is Stichfray production)
Huh
Koma lerolo (yeah) ndikubelani (aah)
Ndikuuzani ine apa ndikubelani (Macholowe)
Manyumba anuo mukangosiya osatseka bwinobwino (Macholowe)
Chitetezo chosakwana (aah!)
Ndikubelani ndikuuzani
(Its your boy Mascot)

Yemwe samadziwa za dzina langa ndani/
Yemwe samadziwa kuti ndimalanga ndani/
Okay n'kufunse chonchi bra/
Unaonako nyumba yopanda ma bagala ba/

Unaonako munthu osaopa akuba/
Ngakhale ku state house kumakhala khoba/
N'khale ma bankinso amaopa ma armed robber/
Tsono choncho wakuba mungamamutenge zoba/
Huh!!!!

Hook
Ndavala nkhwani nkhwani kunkhopeku ndavala mask/
Mmanja muli gun gun pakati pausiku kuhasa/
Ena amanditcha mbava ena kawalala/
Maina ngambirimbiri koma ndimakonda la Macholowe/
(Haaaaaaa!!!!)
Macholowe/
Macholowe/
Macholowe/
Ndine Macholowe/
Macholowe ndine Macholowe/
Macholowe ndine Macholowe/

Manyumba anuo mukangosiya osatseka bwinobwino
Chitetezo chosakwana
Ndikubelani ndikuuzani hahaaaaa

Komatu pena pake ndimakufunilani za bho/
Ndimakondwera mukakhala ndi dola nkuma baller/
Nanga ndingakubeleni bwanji mulibe kanthu/
Nanunso mutha kubwera kuzaba kwathu/

Ine si Zambian koma ndine wo'lusaka'/
Ndili ndichithumba nkona apolisi akundisaka/
Mawa ndizaba kwanu ukakhala ndi soka/
Ndidola zomwezo nkazi wako uja ndisoka/

Kugwidwa ndikoophya komabe sindiopa/
Business iliyonse ndi risk pena imaflopa/
Iliyonseyo ndi dilu bola ndipeze cholowa/
Ndakuuza kale phwanga ndine Macholowe/
Haaaaa!!!

Hook
Ndavala nkhwani nkhwani kunkhopeku ndavala mask/
Mmanja muli gun gun pakati pausiku kuhasa/
Ena amanditcha mbava ena kawalala/
Maina ngambirimbiri koma ndimakonda la Macholowe/
(Haaaaaaa!!!!)
Macholowe/
Macholowe/
Macholowe/
Ndine Macholowe/
Macholowe ndine Macholowe/
Macholowe ndine Macholowe/

Bridge
Palibe anasankha kuti basi ndikhale mbava/
Palibe angakondwe kuti adzishala lova/
Tidzifunse kuti chinamuyambitsa munthuyu ndichani/
Tisanamunyoze kumujaja kaya kumutani/

Outro
Ndikuuza ine apa ndikubelani