Click here to download this song >> Desktop | Mobile
CHANGES (NYASALAND version) LYRICS by Fredokiss
nyasaland aise......nde amati ndi kumpanjetu.....eh! Malawi…..achina fredo aise!
VERSE 1
ZINTHU ZAKE ZINGOKHALA CHIMODZIMODZI AISE/
GWIRA NTCHITO ZAKA ZAKA OSASINTHA AISE/
ATI AKWEZA MALIPIRO SIZIKUSINTHA AISE/
MWINA MWAKE, TIMAFELA KUKHULUPIRIKA/
MAFANA AUVAYA GELE KOMA NTCHITO OSAPEZEKA/
ZAKA ZAKA MAKOLO FEES ANAPELEKA/
MA DEGREE, DIPLOMA, AUTHELA NDENI/
NTCHITO ZAKE AUPASANASO PACHIWENIWENI/
SAAKUPATSA NTAJI OLO UFUNE KUPANGA GENI/
NDIPANGA BWANJI MFANA NDIFUNA NSAMALE STENI/
MFANA WALEMBA ENTRY ANSIYA MBWENUMBWENU/
ZONSE ZINGOFUNIKA MAFANA OZIWIKA/
FUNIKA WINAWAKE AKHALIRE KUMPHIKA/
APO BII! ATI ZONSE SIZICHITIKA/
UMPHAWI WATHU WAFIKA PO PATSILATU STICKER/
UMPHAWI WAMUGHETTO WAFIKATU POSATSIKA/
MAFANA AUBIZIKA BIZIKA MANGOMENYA BANDI
MALUZI ANDIGWIRA NANGA NTANI MPATSE SAA-CHET/
ULULU WACHULUKA U KNOW I GATA CRUSH EEET/
ATI PA RADIO AUKAMBIRANA BU-DGEET/
HOOK
VERSE 2
ZOMWE ZIMACHITIKA ZIMAVUTA KUMVETSA/
UYO ANALI NZANGA KOMA AUFUNA KUNDIGWETSA/
UYO ANALI NDANI KOMA AUFUNA KUNDI KWEZA/
MBEWU ZA NDIMA NDIZOMWETU TIKUFETSA/
BOMA SILI SINTHA AMANGOSINTHA NDI MABEDWE/
ALENJE NDI OMWE AJA ANGO, SINTHA MA PHEDWE/
NKHANI NDIYOMWEIJA YANGOSINTHA MA MVEDWE/
DOLLAR NDI YOMWEIJA YANGOSINTHA MA GWEDWE/
NDALA INALI LOVA PA DENI ETI INKANGOSHALA/
INAPEZA VEPI, PANOPA IMANGOYAKA/
IMANGOYAKA NDI AZIMAYI IMANGO PLAKA/
SIIMAGULA PHWANYA PA DENI IFE SIITIKRAKA/
MA SISTEZ NAWO PANO, AKUTAKATA/
ATI MAFANAFE ATI NDI TSOGOLO LAMAWA/
ZIMAWASANGALATSA TIKATONYOKA NDI BAWA/
UYO ANALI MUNTHU PANO MATENDA AMANGO GAWA/
NDI TIYANA TOMWE PANO MATENDA AMANGO GAWA/
NDI MALUZI AMU GHETTO DOLLAR AMANGOGAWA/
UMOYO WAMU GHETTO PANO AKUNGOKAWA/
KANTSIKANAKA LERO, NZAKEYONSO MAWA/
HOOK
VERSE 3
PA DENI DOLLAR NJE MWINA BRAZ ILOWE JONI/
TINASONKHASONKHA KUTI BRAZ ILOWE JONI/
STENI NGONGOLENGONGOLE BRAZ ILOWE JONI/
2I JULLY IFE TINAMVERA STENI/
BRAZ, SISTEZ, TONSE KUMVERA STEN/
MZUZU ZIPOLOWE NDE TINANGOSHALA NDENI/
THE WHOLE DAY, IFE TINASHALATU NDENI/
BRAZ IUVAYA JONI NDE IFE TISASOKONEZE/
BRAZ IFUNA IVAYE PAJNA IFIKE PA MPOPE/
NDENI MADZI NJE NDE TUUFUNA PA MPOPE/
KOMA PANJA PALIPONSE PALI ZIPOLOWE/
BRAZ IUFUNA IKAFIKETU IKAFIKE PAMPOPE/
APOLISI NAWO PANJA ALI PONSE PONSE/
BRAZ NAYO INANGOGOGOMA KUFIKA PAMPOPE/
INE NDILI PA WINDOW BRAZ ILI PA MPOPE/
RATATATATA BRAZ AISE.....AH!
HOOK
ACHINA FREDO ADA.........
ACHINA FREDO ASIE.........