Jay Jay Cee - Sulingati Enawa [Prod by Gaffar]
Name of album : Sulingati Enawa Genre :Afrobeat
Thumbnail

Click here to download this song >> Desktop | Mobile


virse 1

Hun Pomwe Mwakhalapa pompa apa / Analipo Ena Anka Dzipopa Apa / Ankandiuza Sadzandisiya / Ankati Ndine ndekha amafila / Eh Nawonso Anka Lonjeza / Kuti Sadza Longedza / Anasintha Mawanga / Kundiswera Mtima wanga

Pre - Hook

Anandipekera Dzinkhani / Kundionongera plan / Ndeno Undiudza Chani ? / Pereka Manifesto /

Hook

Kodi Suli Ngati Enawa? / Suli Ngati Enawa? /
Sudzandi Thawa Chikondi Chikukoma baybay. . X2

Virse 2

Nde Nde Nde, Zimene mukunena / Anandiuzaponso Ena / No me No Life / No me No life / Pano Alimoyo / Anawa namiza awo..Anasintha Mawanga / Kundiswera Mtima wanga

Back to Pre - Hook

Back to Hook

Bridge

Ndifuna Kudziwa / Ngati Chikondi Chako Chimapanga Expire / Ndati Undiuze Iweo / Suzanditaya? Ndili Ndi Mantha Ineyo / Ndi Mantha Ineyo / Sindizadzipha Ineyo? .. Nanana