9575Downloads
King Chambiecco - Black Out Again

Click here to download this song >> Desktop | Mobile
Ine ndati sinsekelera izi, Sim'mwetulira ine izi
Aaaaaha !
Kamodzi kawili katatu ! as always mokwezamau pachimkwezamau
Ah king chambiecco, a.k.a zam'bongo
Uthenga uli ndi ka ukali uwu koma mutimvetsese
Yes !Real talk real talk I say
Chorus
Escom kuzangomenya black out again/ black out!
Eti eti eti,eti black out again- pheeeeeing
Water board nayo madzi asiya
Akuti tichita bwanji ife awa, see dem go again
Kuzangomenya black out again/black out!
Eti eti eti,,Eti black out again- pheeeeeing
Water board nayo madzi asiya
Akuti tikhala bwanji ife awa, see dem go again
Verse 1
Aaaaaaha!
Amangothamanga kubwera kudzadula
Mwezi wapita umodzi koma bill yakula
Chifukwa chake nchani uuuuuuko!!!!
Akuti zaDula
Sanafotokoze nkomwe miter azula
Eeehe
Amangonamizira ku nkula awa
Mesa zipangizo amati anagula awa
Nanga bwanji zochita zawo sakukula awa
Awa ndiye takwiya nawo kwambiri
Back to Chorus
Verse 2
Eeeeei
Mwezi watha koma madzi sakutuluka
Zovala tungovala pano zungosuluka
Thukuta kuchita kumata inu lisakutsukika
Chuma kumapeleka koma sizusinthika
Iiiiiiiiiiiiii
Miyoyo yathu siikutukuka
Chiopsezo chachuluka ubwino wapunguka
Kuyera kungochepa,kuda kungochuluka
Kamodzi kawili ah king chambiecco seh!!!
Back to chorus x2 till end