Bathrow - Likamadzatha ft Wakisa James (Zelphy Oldies)
Name of album : Likamadzatha Genre :Hip Hop
Thumbnail

Click here to download this song >> Desktop | Mobile


Intro
(Bathro)
Matthew 24:29 KJV
“After the tribulation of the days shall the days be darkened
The moon shall not give the light
And the stars shall fall from heaven”

Verse 1
(Bathro)
Ndangomva akukamba
Ngakhale osuta chamba
Pakamwa ndi polemba
Dzikoli ndikumwamba
Mfuulo ndi mawu
Akuda ndi mashau
Sizinasiye Mtundu

Ngati moto woyaka
Liwiro ngati zaka
Ngati bomba losweka
Kutembenuza nthaka
Aneneri onyenga
Komanso anamalenga
Kufalitsa nkhaniyi

Chorus
(Wakisa James)
Dziko likamazatha
Lipenga kulira
Zizakhala zowawa
Ulibe Yesu mumtima
Nzanga uzatani iwe
Nzanga uzatani iwe
Dziko likamadzatha
Dziko likamadzatha

Verse 2
(Bathro)
Eti dziko lizatha
Ngati moyonso umatha
Ena kuthatha ndi mantha
Kuvomera kwawo kwatha
Ngati mdima opanda mwezi
Kuzakhalanso zoopsa

Kuganiza mozama
Malingaliro mumtima
Kufatsa ndi mafuso
Ngati mwana osankhwima
Kodi kuzabwera Gorzilla
Mafumuwa kulira
Ndi nkhondo zamumdima
Ngati Hollywood vampires

Chorus
(Wakisa James)
Dziko likamazatha
Lipenga kulira
Zizakhala zowawa
Ulibe Yesu mumtima
Nzanga uzatani iwe
Nzanga uzatani iwe
Dziko likamadzatha
Dziko likamadzatha


Verse 3
(Bathro)
Mayi ubwere utatu
Umwedwe wakwathu
Akaziwa ndi forty
Koma nditenga atatu
Zikukoma chomwecho
Zatulukira zilombo

Ena ali kotamba
Mankhwala akusamba
Magamba akufwamba
Ena mabodza kukamba
Koma bwanji sitimamva
Iyeyo adzabwera ngati mbamva

Chorus
(Wakisa James)
Dziko likamazatha
Lipenga kulira
Zizakhala zowawa
Ulibe Yesu mumtima
Nzanga uzatani iwe
Nzanga uzatani iwe
Dziko likamadzatha
Dziko likamadzatha