4590Downloads
Snag Bomaye - Nyau ft Bwabz & Eagleeye (Prod. Mwanie & Gaffar)
Click here to download this song >> Desktop | Mobile
Verse 1 (Snag Bomaye)
Zalowa zayala nkhutumu kamphasa/
Nabola tadzala mmutumu zidzapsa/
Chimodzi ndimantha, ziwiri mapasa/
Limodzi ndi phata ambiri tatasa/
Mkati mwa bibida zilungamo zadzadza/
Ndi nthawi chabe ah zitisambwadza/
Osautsanza, mtima suvala nsaza/
Tatola zobweretsa bata ndigwire chanza/
Nduvomereza kudikira ndzikhomo/
But u don't need to rush, chitseguka chikhomo/
Dzulo Lavaya leroli ndi dzisomo/
Awawa awowo akudutsa momwemo/
Lunga lunga nkubadwa ndi mau/
Zosekaseka zopusa za ziii mihawu/
Muona nkhanga mipala mashawu/
Ndunena afana obizika kundisemela nyau/
Chorus (Bwabz)
Awa si anzathu/
Tawatulikira, moto tikayatsa iwo amatidzimitsira/
(Nuff ah dem nah real)
Zinyawu amatitsemera/
Ngini zathu iwo amakhomelera/
Tawatulikira, moto tikayatsa iwo amatidzimitsira/
(Nuff ah dem nah real)
Zinyawu amatitsemera/
Ngini zathu iwo amakhomelera/
Verse 2 (Eagleeye)
I'm still going to rap like nobody's business/
Khon'uba iRap ayindibhatali ungena phi?
That's none of your business/
Bohluleka kwi foundation bethela manzi/ ndisokha Not knowing very well ukuba ndim ababemokha/
Ngob'ezingoma ziyokha/
Nibaxelele naba babendi mocker/
Namhlanje ndiya elevate i talk ndiyayi walker/(ha ha)
I started this ndiseyi mveku/
Blessings on the way Ndicela zindithandazeli nceku/
Ndikwazi ubamandla ndingalahli tawuli okwexelegu/
Ndingaze ndi lose patient Ndibe namandla wesihelegu/
Kudala ndagqejw'iNgongoma/
As ba ndikhula ndaqaphela ibingekaqal'INdaba ibiseziNgongoma/
I'm a fan of myself xandi feel pressure kweziye artists ezenzi game ibe shushu I cool my self down/
ndiyazipholisa I will never step down/
To reach my goals I never play foul/
Chorus (Bwabz)
Awa si anzathu/
Tawatulikira, moto tikayatsa iwo amatidzimitsira/
(Nuff ah dem nah real)
Zinyawu amatitsemera/
Ngini zathu iwo amakhomelera/
Tawatulikira, moto tikayatsa iwo amatidzimitsira/
(Nuff ah dem nah real)
Zinyawu amatitsemera/
Ngini zathu iwo amakhomelera/