King Chambiecco - Ndizamugogoda
Name of album : Ndizamugogoda Genre :Dancehall
Thumbnail

Click here to download this song >> Desktop | Mobile


INTRO---ah king chambiecco....kamodzi kawili,,pachimkwezamau basi
As alweys a.k.a zam'bongo ya know,,cyaa one to dem
Uyu ndati nzamu kha kha,,kho kho,,khaaaa,,nzamugagada,,,phwaaaa,,uuuuuko,,aaaaaaha

CHORUS--
akamabwera nzamuboboda,,(bobobo)
Ndizibonga ndati nzamugogoda,,(gogogo)
Uyu nzamukhapakhapa uyu,,(khakhakha)
ndinkhwangwa uyu ndaona sinzanga uyu yes(*2)

VERSE 1--
Azangodabwa kuti diiiiiiiiii,,,ndadina
Cham'mbalimu azangomvera fiiiiii,,ndafinya
Chanthitimu kuti ziiiiii,,ndazika
N'nayenda ndisingano kaya ndaliza
Chapaliombo kuti phwaaa,,,ndaphwanya
Chanmusimu kuti Diiiiiii,,,ndaDina
Osamusiya tsaya phwaaa,,ndaphwanya
Thupi lonse kha khak haaa,,,ndagagada
Ine ndati sinsekelera izi
Kaya ngwankulu koma nzendewera izi
Kaya n'yanzida ine sinlekelera izi
Ah king chambiecco sinmweturilra izi


 


VERSE2--
Ndati nzamuchotsa chimbenene
Nzamuliza nzamumvetsa manzenene
Ngati nguli nzantulutsa manvenene
Nzamuyamba kumutu m'paka chidendene yes(*2)

Mpaka akanene kwa achimwene,,nenene
Kuti ine n'ngwankali ine,,nenene
Osalora zantudzu ine,,nenene
Otamira legeni,,,ine ndemwene

VERSE 3--
Yeeeeeeeeeees bad man afi run away,,athawe athawe
Yeeeeeeeeees wamwanoyo nthana naye uko,,athawe athawe
Athawe lantondo wadooka uko
Akapezeka azondoooka uko
Kamodzi kawiri ah king chambiecco A.K.A zam'bongo
Kaya anthuwa amationa kuchepa masozi
Kaya ndi ukanthitiwu,,koma ulendo uno tithana nawo
Hooooooo ya ya ya ya ziliko kuno