Slessor - Puputa Misonzi
Name of album : Nkhani Za Ku Malawi Genre :Hip Hop
Thumbnail

Click here to download this song >> Desktop | MobilePuputa Misonzi Lyrics Chorus Iwe Puputa misonzi yako/ nthawi yako izakwana/ Iwe puputa misonzi yako/ Ambuye ali nawe cholinga/ Iwe puputa misonzi, Misonzi! MISONZI , misonzi yooo/ Verse1 Ndikudziwa umazifunsa, does God really exist? / is his existence really iust a myth?/ wayesetsa kupempera kwa nthawi yayitali/ panopa ungowona ngati ukutaya nthawi/ aja unkawanena kuti awa ndi otayika/ akunjoya ndi moyo iwe ukungovutika/ ooh U think life is so unfair/ even worse its like nobody cares/ U Cant sleep, ur face covered in tears/ Uli ndi mantha, ur best friend is ur fear/ Kuyesetsa kulimbikira, zinthu osagwira/ Nchifukwa chake mam'mawa umadzuka okwiya/ Koma pali chimodzi chomwe iwe sukudziwa/ chimwemwe chimabwera m'mamawa nde osalira/ Chorus Verse 2 Mavuto omwe timakumana nawo ife tsiku ndi tsiku/ amatikhwimitsa mu nzimu osati nsinkhu/ nde pena mulungu amatha kuzisiya dala/ koma sikuti amakhala abuye atiyiwala/ Anthu omwe unkawadalira anakutaya/ nakutcha bulutu kape, mphawi nde kazivaya/ koma anthu omwewo ndi amene azakutame/ ali sister please tandigayileni money/ Pamenepo iwe utayiphula zikuyenda/ ukuthandiza ana amasiye ndi amatenda/Nde chonde mukamanyoza anzanuwo muzidziwa/ mulungu si jemusi mawa ndi tsiku lina/ Chorus Bridge Mulungu samawona nkhope/ M'mbale wanga usatope/ I know he's got planz for u and and and u and u/

 • Malawi-Music Blog

 • ABOUT

  Through this portal, Malawi-music.com provides you with the lyrics of the top songs in Malawi.

  This is your number 1 spot for up-to-date lyrics of the latest top songs in the country

  Visit Malawi-music.com to download more songs from your favourite local artists.

  Visit the Malawi-Music Blog to get the latest news updates on what's happening in the music industry.

  And also Checkout videos.malawi-music.com to watch and download the top videos in the country.

 • Other Links

 • Malawi News

Malawi Music Lyrics by Malawi-Music.com