9455Downloads
Singlay - Ndakusowa

Click here to download this song >> Desktop | Mobile
Its your boy Singlay
VERSE 1
Chimwemwe changa nthawizina chimadzabwelera m'mbuyo
Makamaka ndikakumbukira nthawi yomwe takhala limodzi
Ndithudi sindinkaganizira kuti ungadzachoke chonchi
koma chinachake chimandiuza kuti uli ku paradizo (paradizo)
CHORUS
Ngakhale ndikudziwa uli pabwino koma ndakusowa-ah
Ngakhale ndikudziwa uli pabwino koma ndakusowa
Iwe ndakusooowa ndakusowa-ah x2
oh noh
VERSE 2
Ndikamakhala nthawizina ndimangokhetsa misonzi
makamaka ndikakumbukiraaah zoti iweyo unapita
Kungochoka osatitsanzika? Kodi kukhala amatero?
Chonchobe poti ndi chikonzero cha mwiniwake Mulungu
CHORUS
Ngakhale ndikudziwa uli pabwino koma ndakusowa-ah
Ngakhale ndikudziwa uli pabwino koma ndakusowa oooh
BRIDGE
Ndikuyenera kudziphunzitsa kumwetulira nkamayang'ana chithunzi chako
poti padzikolino palibe wamuyayaaaaaaaah!
Ndikuyenera kusiya kulira poti chiyembekezo chilipo oh
kuti tsikulina tidzaonanaah
CHORUS
Iwe ndakusowa x4
Ndakusowa x2
Oh noh x 5