Mascot - Kodi Bwanji (Prod by BFB and MBJ)
Name of album : G.L.C (Good Luck Charm) Mixtape Part 2 Genre :Hip Hop
Thumbnail

Click here to download this song >> Desktop | MobileIntro It's your boy Mascot/ Yeah/ It's your boy Mascot/ Kodi Bwanji Nkazi Kodi Bwanji/ Kodi Bwanji Nkazi Kodi Bwanji/ Kodi Bwanji Nkazi Kodi Bwanji/ Kodi Bwanji Nkazi Kodi aaaahh/ Hook Kodi Bwanji Nkazi Kodi Bwanji/ (Kodi Bwanji) Kodi Bwanji Nkazi Kodi Bwanji/ Kukonda dollar chonchi ngati Bushiri ndi mdala yako/ Kukonda dollar chonchi ngati Salanje ndi mkozi yako huh!!!/ Kodi Bwanji Nkazi Kodi Bwanji/ (Kodi Bwanji) Kodi Bwanji Nkazi Kodi Bwanji/ Kukonda dollar chonchi ngati Bushiri ndi mdala yako/ Kukonda dollar chonchi ngati Salanje ndi mkozi yako huh!!!/ Verse 1 Kukonda kugwiragwira dollar ngati bank teller/ Mpakana dollar zanga zonse wandithera/ Sitingatchile bhobho basi undipemphe mayunitsi/ Uli tabwera tikumane pa lunch tikadye Kips/ Zandilaka wachulukitsa ma demand/ Sungandibele ndikuona you know am not blind/ Day light robbery ndiyomwe ukupangayi/ When ever I go broke ukuvaitsananso ndi mzangayi/ Uzibwenza zanga zokha uzibwenza/ Ndikuphika ndikuphaka ndikumeza/ Dollar zanga ndavutikila kuzipeza/ Ukapanga chibwana iwe ndikukhweza/ Uzibwenza zanga zokha uzibwenza/ (Uzibwenza) Ndikuphika ndikuphaka ndikumeza/ (Ndikumeza) Dollar zanga ndavutikila kuzipeza/ (Whaaattt!!!) Ukapanga chibwana iwe ndikukhweza/ Hook Kodi Bwanji Nkazi Kodi Bwanji/ (Kodi Bwanji) Kodi Bwanji Nkazi Kodi Bwanji/ Kukonda dollar chonchi ngati Bushiri ndi mdala yako/ Kukonda dollar chonchi ngati Salanje ndi mkozi yako huh!!!/ Kodi Bwanji Nkazi Kodi Bwanji/ (Kodi Bwanji) Kodi Bwanji Nkazi Kodi Bwanji/ Kukonda dollar chonchi ngati Bushiri ndi mdala yako/ Kukonda dollar chonchi ngati Salanje ndi mkozi yako huh!!!/ Verse 2 Ndikanakhala mfana wa mphwiyo bwenzi ndikunvetsa/ Koma ndine kapolo ndimachitila kukhetsa/ Thukuta/ Kuti ndipeze dollar zimavuta/ Nkapeza Ka grand nde kuti mfana ndaswetha/ Sendera pafupi umve chinsisi/ Ndine mfana wokhwima wamitsitsi/ Kadola kangako ukapanda kukabwenza/ Nkulumbira ine apa ndikulodza Aaaah!!/ Uzibwenza zanga zokha uzibwenza/ Ndikuphika ndikuphaka ndikumeza/ Dollar zanga ndavutikila kuzipeza/ Ukapanga chibwana iwe ndikukhweza/ Uzibwenza zanga zokha uzibwenza/ (Uzibwenza) Ndikuphika ndikuphaka ndikumeza/ (Ndikumeza) Dollar zanga ndavutikila kuzipeza/ (Whaaattt!!!) Ukapanga chibwana iwe ndikukhweza/ Hook Kodi Bwanji Nkazi Kodi Bwanji/ (Kodi Bwanji) Kodi Bwanji Nkazi Kodi Bwanji/ Kukonda dollar chonchi ngati Bushiri ndi mdala yako/ Kukonda dollar chonchi ngati Salanje ndi mkozi yako huh!!!/ Kodi Bwanji Nkazi Kodi Bwanji/ (Kodi Bwanji) Kodi Bwanji Nkazi Kodi Bwanji/ Kukonda dollar chonchi ngati Bushiri ndi mdala yako/ Kukonda dollar chonchi ngati Salanje ndi mkozi yako huh!!!/ Kodi Bwanji Nkazi Kodi Bwanji/ (Kodi Bwanji) Kodi Bwanji Nkazi Kodi Bwanji/ Kukonda dollar chonchi ngati Bushiri ndi mdala yako/ Kukonda dollar chonchi ngati Salanje ndi mkozi yako huh!!!/ Kodi Bwanji Nkazi Kodi Bwanji/ (Kodi Bwanji) Kodi Bwanji Nkazi Kodi Bwanji/ Kukonda dollar chonchi ngati Bushiri ndi mdala yako/ Kukonda dollar chonchi ngati Salanje ndi mkozi yako huh!!!/ Kodi Bwanji Nkazi Kodi Bwanji/ Kodi Bwanji Nkazi Kodi Bwanji/ Kukonda dollar chonchi ngati Bushiri ndi mdala yako/ Kukonda dollar chonchi ngati Salanje ndi mkozi yako huh!!!/

 • Malawi-Music Blog

 • ABOUT

  Through this portal, Malawi-music.com provides you with the lyrics of the top songs in Malawi.

  This is your number 1 spot for up-to-date lyrics of the latest top songs in the country

  Visit Malawi-music.com to download more songs from your favourite local artists.

  Visit the Malawi-Music Blog to get the latest news updates on what's happening in the music industry.

  And also Checkout videos.malawi-music.com to watch and download the top videos in the country.

 • Other Links

 • Malawi News

Malawi Music Lyrics by Malawi-Music.com