Phyzix - Nazo
Name of album : Nazo Genre :Rap
Thumbnail

Click here to download this song >> Desktop | Mobile


*NAZO Lyrics by Phyzix*

*INTRO*
Politics/ Conflicts/ Mabebi/ Maluzi
Politics/ Conflicts/ Mabebi/ Maluzi

*VERSE 1*
Ndimadya thukuta langa/ ndine chimfana cha umve/ zachibwana sindimapanga ndine kapolo sanakuuze/ tanena kuti tikumve zomwe zimavuta kuti utimve/ ndife mafana a kalekale tinawerenga Tsala ndi Timve/ ma vote nde timaponya koma tikumadyabe zi bonya/ a ndalewa ndi mabebi ndi amene akumapanga zobhowa/ amabwera ndi ma heart break mphwanga utha kuphowa/ zikati zafika mbola palibe zokuti ndiwe chiphona/ ndatopa nazo

*HOOK*
Ndatopa nazo/ ndatopa zazo
Ndatotopa nazo nazo
Ndatopa nazo/ ndatopa zazo
Ndatotopa nazo nazo
Politics/ Conflicts/ Mabebi/ Maluzi
Politics/ Conflicts/ Mabebi/ Maluzi

*VERSE 2*
Sizikupanga chipongwe anthu panopo si zi kufwamba/ ndatopa kuphula njerwa ndikufuna ndizatole chikwama/ struggle mu ghetto si ti ma kazinga chakudya timawilitsa/ water mu kettle ku yi khwidzinga kenako madzi kuphitsa/ ukwati wa dzulo uja kucha kwa lero akuti watha/ ndalama za chipatala zija akuti aba zatha/ zaka zaka zikupita koma moyo osamasintha/ bolanso weather umadziwa kuti summer kenako winter/ ndatopa nazo

*HOOK*
Ndatopa nazo/ ndatopa zazo
Ndatotopa nazo nazo
Ndatopa nazo/ ndatopa zazo
Ndatotopa nazo nazo
Politics/ Conflicts/ Mabebi/ Maluzi
Politics/ Conflicts/ Mabebi/ Maluzi

*BRIDGE*
Ndatopa nazo/ ndatopa ndatopa zazo

*HOOK*
Ndatopa nazo/ ndatopa zazo
Ndatotopa nazo nazo
Ndatopa nazo/ ndatopa zazo
Ndatotopa nazo nazo
Politics/ Conflicts/ Mabebi/ Maluzi
Politics/ Conflicts/ Mabebi/ Maluzi