Blaze - Mtima (Prod. Jay Emm)
Name of album : Mtima Genre :Afro-Pop
Thumbnail

Click here to download this song >> Desktop | MobileVerse 1 Lero ikhala finals Undiuze umaona chani mwa ineyo Ukamanditreater chonchi Umati ndine ndani kwa iweyo Kodi mesa amati m`modzi mwa ifeyo Anachokera kunthiti ya nzache Ndikudabwa kuti m`modzi mwa ifeyo Salabadira mkomwe zanzache Bridge Zizikomera mbuzi kugunda galu chikondi chanji darling Kukhumudwitsa nthiti mtima uli m`malo umakwanitsa bwanji darling Chorus Kukonda iweyo, sikuti ndikupusa ayi Ndikamakupepesa, sikuti kusatira khusa zako Koma mtimaaa, mtima wathu uzatipusitsa ife Abale chikondiii, chikondi chathu chizatipwetekesa ife Tisafele mphathi Verse 2 Ayi ndisaname sweet inu, inu mwanditora pamudzi pano Ngati kuti mwina ine ndilibe kwathu Mwanditora pamudzi pano Ine ndikalakwa ndimapepesa Koma ayi mpakana suspension Mukalakwa ndimamvetsetsa Munthu sangalakwire mtengo Bridge Zizikomera mbuzi kugunda galu chikondi chanji darling Kukhumudwitsa nthiti mtima uli m`malo umakwanitsa bwanji darling Chorus Kukonda iweyo, sikuti ndikupusa ayi Ndikamakupepesa, sikuti kusatira khusa zako Koma mtimaaa, mtima wathu uzatipusisa ife Abale chikondiii, chikondi chathu chizatipwetekesa ife Tisafele mphathi Bridge Usazuze mtima Usazuze mtima Usavulaze mtima wa ine Usazuze mtima Usazuze mtima Usazuze mtima Usavulaze mtima wa ine Usazuze mtima Kodi mesa amati m`modz mwa I ifeyo Anachokera kunthiti ya nzake Ndikudabwa kuti m`modzi mwa ifeyo Salabadira mkomwe zanzake Chorus Kukonda iweyo, sikuti ndikupusa ayi Ndikamakupepesa, sikuti kusatira khusa zako Koma mtimaaa, mtima wathu uzatipusisa ife Abale chikondiii, chikondi chathu chizatipwetekesa ife Tisafele mphathi

 • Malawi-Music Blog

 • ABOUT

  Through this portal, Malawi-music.com provides you with the lyrics of the top songs in Malawi.

  This is your number 1 spot for up-to-date lyrics of the latest top songs in the country

  Visit Malawi-music.com to download more songs from your favourite local artists.

  Visit the Malawi-Music Blog to get the latest news updates on what's happening in the music industry.

  And also Checkout videos.malawi-music.com to watch and download the top videos in the country.

 • Other Links

 • Malawi News

Malawi Music Lyrics by Malawi-Music.com