21625Downloads
Malinga - Click One - Mupange Zanu Muyese (ft Malinga Mafia) (Prod Dj Sley)

Click here to download this song >> Desktop | Mobile
jia (why we there?)
click (click-one and the general)
yes (mafia)
wat (why we there?)
(hook) Malinga Mafia
Mupange zanu muyese
deal yazanu musanaphweketse
nkhalidwero!
lopusali tilithetse mafana pa gulu zida musamayese ah
mupange zanu muyese
deal ya zanu musanaphweketse
nkhalidwero!
lopusali tilithetse mafana pa gulu zida musamayese Yo
(verse1) Click-One
kwa yese amayesa amadziwa ndizotheka
kwa omwe samayesa samadziwa ndizophweka
amachivutitsa chithu choti ndichophweka
amachiphweketsa chithu choti ndichovuta zausiru eti?
kumamuthoka munthu hule oti sunayese ngati size
mwangokumana pa Mbowe sunafunse olo price
sunalowetse mkomwe koma mkumati ikuthina
sunaimalize mkumati ufuna nsima ina
iwe thumbidwa eti?
zaufiti eti?
osamuthoka munthu mfiti ngati sunagwire
mkumati anabwera usiku kuti andigwiregwire
chani? (umu)
china? (apo)
hah?
osathoka dala kuti ndiyoshupha ngati geri
sten ndiyovetsetsa ngati phone blackberry
udzayitulukira tsiku lina ungoyesa!
(hook)
Mupange zanu muyese
deal yazanu musanaphweketse
nkhalidwero!
lopusali tilithetse mafana pa gulu zida musamayese ah
mupange zanu muyese
deal ya zanu musanaphweketse
nkhalidwero!
lopusali tilithetse mafana pa gulu zida musamayese Yo
(verse 2) Click-One
kwa onse sanayese kwa ineyo ndikamwana( juu!)
ine ndinayesa panopaso zinamkwana (size)
ndikudyaso bho plus kumeta bho zayamba kuthinano skin jean
khole p square colabo kuti m'bise izi
ziti?
mavu iwe!
uli zii
osaphusha ngini umangodikira chilichosecho kwa masten
ulibwanji iwe?
sindukupatsa moni koma uganize fast
sungamapephe dollar kwa masten yogulira pant
pamodzi ndi tchiki yako mukukhala ngati one part
pezani chochita man muyaluka town muno ngati mkeka iwe!
uzipha makwacha a police samamanga
amangokudinyadinya akakupeza ukuthanga
ngati mu september mphwanga
anamponda nthanga
mwina uyesere iweyo utha kukwanitsopanga
(hook)
Mupange zanu muyese
deal yazanu musanaphweketse
nkhalidwero!
lopusali tilithetse mafana pa gulu zida musamayese ah
mupange zanu muyese
deal ya zanu musanaphweketse
nkhalidwero!
lopusali tilithetse mafana pa gulu zida musamayese Yo!
(outro) Malinga Mafia
Yo! Click-one and the general mafana samadziwa me shine
me gone *** badest combination run up this nation