54988Downloads
Sir Patricks - Ndife Ana Anu (Prod. Pon G)
Click here to download this song >> Desktop | Mobile
Ndife ana anu
Ndife ana anu
Msatilore tisauke
Ndife ana anu
Ndife ana anu
Msatilore tivutike
Verse 1
Malawi dziko langa lokondeka ah
Lomwe ndinalikonda ndili mwana ah
Koma zambiri zapotoka
Zaloza kuzende
Chonde mbuye, unikilaaanipo
Chuma chathu ngati dziko mchofooka
Anthu ambiri dziko langa ngaumphawi
Mene muchilitsa China
Mudalitsa America
Naye Malawi mumkumbukireee
Chorus
Ndife ana anu
Ndife ana anu
Msatilore tisauke
Ndife ana anu
Ndife ana anu
Msatilore tivutike
Verse 2
Zotupa zamubongo komaso m`mimba ah
Bp cancer komaso sugar ah
Imfa za amayi apakati
Ana ogwiliridwa, odwala edzi
muakhudze ndinuuuu mbuye
Sambitsani misewu yathu ndi mwazi wanu mbuye
Ngati tachoka amoyo tikafike
Dalitsani atsogoleri, amipingo azipani atilamulire
Umo mufunila halleluyah
Ndikamaliza ntchito yanga, yoimbayi
Ndizatseka maso, ambuye adzandiitana
Ndiye otsalanu, musazatope, kumpemphelera
Malawiii
Chorus
Ndife ana anu
Ndife ana anu
Msatilore tisauke
Ndife ana anu
Ndife ana anu
Msatilore tiyaluke
Bridge
Mbuye malaawii
Dziko langa, dziko langa
Dalitsani Malaawii
Dziko langa, dziko langa
Chorus
Ndife ana anu
Ndife ana anu
Msatilore tisauke
Ndife ana anu
Ndife ana anu
Msatiloere tivutike