Alinafe Jimu - Akutsata Kutchipa
Name of album : Time is money (Live Acoustic) Genre :Acoustic
Thumbnail

Click here to download this song >> Desktop | Mobile



Chorus


Akusata kutchipa x3 ee!
Mukuzitchipitsa nonkha x2

VERSE ONE


Sionse amakufunsila chifukwa chakukongola, ambiriwa akusata kutchipa.
Pakuti wena kufunsira kumamwavuta, sono inu m’mangopereka ma cotation.
Koma mukuzinyasiraniji?? akazi abwino oyenera pa banja ngati inu.
Ine chikundinyas simukuona saizi, mukumavulira tiwana.
Akuti wakwatila waluza, akazi amasikwano alibe mwini
Akuti kukana  amuna ndi ntchimo, koma kumangololla aliyense bola ndalama 
Komabe

CHORUS


VERSE TWO


Ndiwe mkazi wamtundu wanji? Makani ngati makaniko wa fegi.
Uhule  omwewu m’paka kuvalira worksuit,
Wati unafa kale zako zinada.
Lero waitenga ngati profitable business,
But you don’t know what will happen tomorrow.
Siku lina sundaufunanso, utawonda ngat nthiko ophikira m’memo.
Makolo ena okutha mapulani, amatuma ana awo azipanga uhule.
Eti kumachita kuwapasa target ngati minibus,
Lero ndi izo wabweretsa matenda. Musadabwe!!

Chorus


VERSE THREE


Zoti kuli matenda alibe nazo ntchito, iye kwake ndikudabulisa amuna.
Amanena monyada ali asafuna asiye, ati jelasi people never win.
Mabanja akale an’kati akafunsirana, chaka chimatha asanalolane.
Koma lero ndizapompo pompo kuthana kuthana
Akunmango kuudza ndalola koma ndilandiliretu (Ambere chire bola change!).

Chorus