Blakjak Che-Kalonda - Dr Che [Prod. Desert Eagle & Sispence]
Name of album : Dr Che Genre :Dancehall
Thumbnail

Click here to download this song >> Desktop | MobileIntro Mmh Current situation.. Yeah man.. you Blakjak Indee.... you Desert Eagle, Sispence Akazi Akufuna Dr. Che Whaaaaayahsayyy Indee... Chorus Ati.. Ati Sakufeela bho Akumva fever Komanso Malungo Nde Akufuna Dr. Che Am'baye Dr. Che Am'baye x2 Verse One (Eyoh Eagle) Anabwera Kwathu dzulo Kufikila kulowa Ndili mtulo Kenako Nkudzakoka Ka Pillow Mmnh, Basi pompo tulo Mmwawa Podzuka Akukhetsa msonzi Zatheka Bwanji kuti zifike Chonchi Thupi latenthelatu ngati Patient Oooh God! Latentha ngati patient Verse Two Ati Wadwala Akufuna achile Wakhalira Kugona Akufuna Ayime Adye zipatso komanso Avine Mwezi uwale tisewere Tiimbee Komatuuuu,, Siine doctor poti Nkakubaya poyipa sulira Moti Ati Nzabhobho Kuyankha Mwakhonfii Mmmmm Akuchita Kuyankha Mwakhonfii Verse Three Panopa Nkhani yashupha Ndikungoyenda modumphadumpha Ndinamm'baya nde Watupa Angotulukanso Thukuta Apa nditani Ase Akazi Onse angofuna Dr. Che Komatu Ine ndilibe licence Nditha ndine Nzanu Sispence Chorus Outro

 • Malawi-Music Blog

 • ABOUT

  Through this portal, Malawi-music.com provides you with the lyrics of the top songs in Malawi.

  This is your number 1 spot for up-to-date lyrics of the latest top songs in the country

  Visit Malawi-music.com to download more songs from your favourite local artists.

  Visit the Malawi-Music Blog to get the latest news updates on what's happening in the music industry.

  And also Checkout videos.malawi-music.com to watch and download the top videos in the country.

 • Other Links

 • Malawi News

Malawi Music Lyrics by Malawi-Music.com