1488Downloads
Satoh - Kalikiliki
Click here to download this song >> Desktop | Mobile
Lero kalikiliki/
Lero lokha kuli kalikiliki/
Lero kalikiliki/
Lero tigona koma pankitikiti/x2
Verse 1
Wantali likiliki
Wamfupi likiliki
Oonda likiliki
Onenepa likiliki
Lero tikoka ma chick chick
Ndati tikoka ma pretty pretty
Bawa iliko zikwizikwi
Dance yake sick sick
Fans kutenga ma pic pic
Bwera titenge chi pic pic
Ndingobwera mwa peace peace
Simafana ama kick kick
Palibe zomavaya pretty
Mpakana titathana psiti
Itanako anzako 50
Ndabwera ndi mamemba 60
Hook
Lero kalikiliki/
Lero lokha kuli kalikiliki/
Lero kalikiliki/
Lero tigona koma pankitikiti/x2
Verse 2
Wantali pokopoko
Wamfupi pokopoko
Oonda pokopoko
Onenepa pokopoko
Town yonse pokopoko
Line yonse pokopoko
Phazi liri dokhodokho
Vina ngati bokhobokho
Atagone zakezake
Aliyense wakewake
Ndati yense chakechake
Palibe andisakesake
Wamng'ono sangamake
Akayamwe kwa make
Tulo lero lindilake
Wina mpaka italakwe
Hook
Lero kalikiliki/
Lero lokha kuli kalikiliki/
Lero kalikiliki/
Lero tigona koma pankitikiti/x2